Email a copy of 'DPP’s Ngwenya handover maize mill to Area 23 residents: Free to all ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Jamax
Jamax
6 years ago

That’s the only way to go nowadays kkk now let MCP open up shops giving out free Laundry soap and free Sugar, PP to bring back free kabaza transport for everyone, UDf to bring about free shoes for everyone, PPM to bring free Axa bus transport, AFORD to bring about free lobola for any man who want to marry from the North kkkkkk!!!!

Zachamba
6 years ago

Anthu a ku area 23 landirani chigayo, koma vuto ndi lakuti magetsi ku Malawi kuno a dpp akukanika kutipatsa. nanga chigayocho chiziyendera chiyani??? Komanso landirani chigayo chomwe chagulidwa ndi ndalama zanu zomwe a dpp akhala akukubelani. Ngati agawe ndalama landirani mumudyere ndalazo ndi zanu zomwe agalu amenewa akhala akukuberani. Koma chofunika muwaonetse kuti voti iri mu mtima. Msungama ndiye munthu wofunika kumuvotera.

Kandideti
Kandideti
6 years ago

stone age donations

Gogodasi
6 years ago

wa Jeffrey, you must know the roles of an MP and a Councillor. An MP does not need to be responsible for development because that task is for the Councillor while MP’s responsibility is to make good laws in the National Assembly. What you are saying simply demonstrates your total ignorance and you cannot separate the responsibilities of an MP and a Councillor. I am not surprised you are bribing voters with a maize mill. Why did you not give them the maize mill two years ago and you are doing it now? Mind you people are not fools, they… Read more »

Matako
Matako
6 years ago

I thought the guy was smarter than this. Philip Bwana tried the same shit in 2004 and lost miserably!

santana
santana
6 years ago

Kupepera kwa anthu kuonekera pa chisankhochi. Achewa amati papas tonora sudziwa mtima wamoto. Ndani amafuna phungu wake kukhala wa opposition m’mene kumapwetekera kotsutsa? Ndiye munthu ukudziwiratu kuti munthuyu ali chipani chotsutsa ndiye iwe nkumataya voti yako mwaiyeyo? Tamufunsani Chakwera akuuzani m’mene kumapwetekera kotsutsa. Makamaka pakali pano pomwe akudziwiratu kuti 2019 chakenso palibe ngakhale ena akuyesetsa kumamulimbitsa mtima kuti anthu wonse azipani zina ndianu bwana. Funso langa kwa Chakwera: How many districts in the southern region have you convinced to vote for you, and mention the districts? Why do you think some central region districts voted for DPP in 2014, a… Read more »

citizen
citizen
6 years ago
Reply to  santana

Santana, you seem to have deep knowledge of Malawian politics than most people.

Patrick Phiri
Patrick Phiri
6 years ago

Ngwenya is a true leader. He knows what his people want, and he provides. A great leader he is. Be aasured of my vote.

Remnant
Remnant
6 years ago

Zomvetsa chisoni kwabasi…. Chigayo chakecho chakuthaithanso. Ndiye poti muchizula pa 20 October pano mukaluza palibe vuto. Campaign style ya achair imeneyo. Zachikale basi. Koma chaka chino mudziwanso. Musiya zopusazo.

zonkE
zonkE
6 years ago

kkkkkkkkkkkkkkkkk after 23 years of multiparty system

Bwatha
Bwatha
6 years ago

koma abale the whole os SG kukapeleka Chigayo zoonaaa.aaaa

Read previous post:
Kamuzu Barracks title defence collapse

Malawi’s flasghip TNM Super League defending champions, Kamuzu Barracks have relinquished their hopes of defending the league following their poor...

Close