Email a copy of 'DPP's 'sesa, sesa’ orator Saonda in bribery scandal' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Ovilhelha Chaponda Chimanga
Ovilhelha Chaponda Chimanga
6 years ago

Saonda ndiwoyerekedwa, greedy & a crook!

Amaduh Cassim
Amaduh Cassim
6 years ago

search me

kas
kas
6 years ago

Jeffrey mumalimbana naye chisoni msiyeni Dada waku nkhotakota adyerere ndale za Dpp ndimzimayi olimba ameneyu kugwetsa makhang’a pa ndale kaka Dr chilumpha(former VP),komaso Fahad Assan amene anali senior minister nthawi ya amai simasewera ayi muzimupatsa ulemu,moreover she is from central region… Dada musafoke mupitirize kugwira ntchito molimbika ndimokhulupirika

Nduzayani
Nduzayani
6 years ago

kodi inu a dpp mukamapereka udindo kwa munthu mumafuna chikhale chowopsezera?pano saonda akuopseza anthu ndipo nthawi zonse amayankhula kuti iye amafika pali ponse moti akuti ngakhale Peter amanvera iye.Dpp thandizani anthu omwe anavota saonda watikwana

Zokoka
Zokoka
6 years ago

Mjcentral, you are right. Awaombe kumene. Amene muli madolo tawadyereni amwenyewa. Akutiyenjeza agalu amenewa. Wabwera bhooo sesa sesaaaa

mtete
mtete
6 years ago

I am not surprised at all. Activities such as Saonda’s are perfectly normal in DPP.

As for Jeffrey, my advice is for her to get out fast. Positions like hers are for DPP’s sacred cows from the Lhomwe belt or, if anything at all, from South.

Malawian Mwanavava
Malawian Mwanavava
6 years ago

DPP paulendo

Zicheche
Zicheche
6 years ago

Akhakhakha, ikanakhal MCP bwezi muli ng’we-ng’we-ng’we apa….
shupitiiiiiiiii!

Mjcentral
Mjcentral
6 years ago

Kodi amwenyewo amafuna chiyani kwa President wathu wokondeka?? Kuzolowera katangale basi….. Azikudyerani choncho.

Read previous post:
NICO boss slapped for  flirting with Doctor’s wife

Newly appointed Nico Life Chief Executive Officer Eric Chapola had a rude awakening on Sunday evening when he was slapped...

Close