Email a copy of 'DPP's Wa Jeffrey calls Malawi Law Society condemnation as 'Zachamba':'Blue Night' parastatal money' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nkhwiri inokwa
nkhwiri inokwa
6 years ago

kodi mayi amenewa anayendapo mu bar as hule eti,,,,,she seems all the tym kuti she cant reason and this man amangoyankhula mamina ali mmutu kodi mesa mukuti ndi DR munthuyu kkkkkkkkk ma DR akumalawi basi sindizakhala DR shaaaa

Juju Malema
Juju Malema
6 years ago

kodi mmesa kukubwera ina akuti BEAM chitenje chani chani ma parastatal akufunika kuti agule ma tables nde mudzati cha Dii Phii Phii boma ilo

santana
santana
6 years ago

Kodi munthu wamkazi mukubwata naye m’mimba chonchi bwanji? Mkaziyutu akamamva chonchi amasangalala amangoti azimuna ndawamvetsa m’bebe. Masiku aja munkamva m’bebe ndi Kaliati lero ndi wa Jeffrey.

PapaChalo
PapaChalo
6 years ago

Jeffrey, you are out of your mind. Kodi amabungwe, ACB etc osamukumbutsa ndalama anaba za education ma constructions a masukulu. our courts and other related organisations are too weak. Maybe they were under trained.

Ngulenjeti
Ngulenjeti
6 years ago

Mkazi amend mumati Wa Jeffrey yo kosi anapengapo nthawoli zose amayankhula ngati Wa Ku st johns hospital or Ku mental Ku zomba za. Amutab ndani aziwa kuti anaduka kale mutu kungoti kkkkkk

Raw Stuffer
Raw Stuffer
6 years ago

Something terrible is trailing the blue camp. Someone who was begging for assistance can not be as blatant as Ntaba and DPP Secretary General have been of late. Wait. This is gonna blown up soon.

ADE
ADE
6 years ago

KU LILONGWE WANTHU WAKUMWA MAVI

Mahera
Mahera
6 years ago

I don’t think the issue is about PAC here, we are talking of the party that is busy plundering our resources. Jeff and Ntaba must know that they don’t own Malawi. One day they will face the music.

Maunits
Maunits
6 years ago

Kodi iwe Kalupa a Frobarometer omweaja abalosera kuti dpp yiwina 2014 an enanapo kuti dpp yiwina 2019 kapena MCP ndi Lazarus Chakwera akuwina titati tiponyemavoti now. Kalupa ndikuvera chisoni chifukwa ukuganiza kuti dpp yingawineso ukanakhala wina bwezi sikunena motero kuopa kuchitidwa manyazi. Wolosera ena anenaso kuti amene awine Nsanje Lalanje ndi Lilongwe City South East ndamene ati atole chikwama 2019. Ndiye musaalankhule zambiri khalani chete mungatinyasepo apa.

Kharupa
6 years ago

By the way, Why did PAC meet Chakwera alone to discuss 2019 elections? Why did they conduct their discussions in hiding? Kodi pa half-time, REFEREE amakalowa mu dressing room ya team ina? How can the other team behave towards that kind of referee? PAC is giving false hopes to chakwera and this shall make him to have difficulties to accept a loss in 2019. PAC should be careful not to create that king of anticipation. Please!!!!!!!!!!!!

PAC must invite all parties when discussing national issues. Amakagawana masikono ku MCP eti!!! Shupiti

Becks
Becks
6 years ago
Reply to  Kharupa

Khoropa is this comment in line with the article? Anyway get back to the PAC meeting. PAC is doing consultations with stakeholders including government. The consultations are not about 2019 General elections but on Local Government Act that governs district and town councils. Get things right

mathews malata
6 years ago
Reply to  Kharupa

Join the discussioniwe wachibwana eti??? muja amapangila mwano kasaila angakakhalenawo pamsonkano wa PAC??? take note that anthuwa amaitanidwa onse koma enawo amachita kukana,,, ndi anyapapi kk

Read previous post:
Minister warns contractors of substandard work, they risk licenses revoked

Minister of Transport and Public Works, Jappies Mhango has issued a stern warning to contractors in the country against indulging...

Close