Email a copy of 'Drama as fan is seen peeing on the goalposts' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

22 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
eston bryson
eston bryson
6 years ago

Tionanana loweruka

eston bryson
eston bryson
6 years ago

Tiona Saturday kuti azatan!!

Sean Mady
6 years ago

Koma ku Malawi ndiye tikuyaluka nazo izi!!! A wanderers kukhulupilira nyanga too much. last time anapaka mafuta a nkhumba ku Blantyre. Anyway flames yathu sizapita patali.

bigman munthu waMulungu
bigman munthu waMulungu
6 years ago

muti in action kkkk

nomad
nomad
6 years ago

KASOVANI IFE ON SAT. FINALS PANO ILI MMANJA 5MITA WETHER WE LOSE, UMBONI WA ANANUUUU? KAGWEREN UKO. MUKATENGE ANU, ENA MUPATSE FLAMES (SIIDZAMVA) A BAD CARPENTER BLAMES HIS TOOLS. KKKKKKKKK! UKO KUNALI KULIRA KWA NDAN PAJA?

nomad
nomad
6 years ago
Reply to  nomad

MIKODZO IMASULUTSATU SIMASEWERA, USALIRE NEBA IWE PA EASY PA THABWAPO, WAIT UONERE BALLS YOKOMA SI ZA MADUNYU ANU AJA, MPAKA RVG ANATHAWA GAME YANU!

TRUTH
TRUTH
6 years ago

Uchitsiru. I can’t support timu ya anthu okodza ndikunyera mu ground. Nyerere zonyera pali ponse.Savages!!!

Rigobert
Rigobert
6 years ago

Ma steward akwathu kuno sadziwa ntchito yao. I dont know who trains them, amaonera mpira pomwe a maiko ena amayang’ana ku ma stand koma athuwa maso tudzu mground akachinya uwaona akujowa nawo kkkk I dont think they will write any report poti izi sanaone pomwe zimayambira for Vales is a total shame

Cos
Cos
6 years ago

Hahaha kuli Nyerere ku manoma! Simunati mumva m’bebe

wengie
wengie
6 years ago

Kodi anakodza kapena ayeserera kukodza?

Mmmmmvkoma mpirawu ndiye wafikadi povuta

waves
waves
6 years ago

Apolice kumangoyang’ana??????????

Read previous post:
Opposition will be there, but God will deliver his children

Many times God’s children have been in situations that do not look good at all. These are some of the...

Close