Email a copy of 'Drug Fight Malawi wants Nyasa Tobacco company out of Bullets FC' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

104 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
stevie phiri
stevie phiri
8 years ago

vuto lili kuno kumalawi ndilakuti timalolela kulanda ndalama kwa athu ena ndicholinga mukasokoneze zithu zimene zikhoza kutukula malawi .apa zaonekeratu kuti zomwe akupanga mr nelson zakeyo atumidwa ndi anthu ,koma chomwe mungaziwe mr zakeyu mukutaua nthawi ndizimenezi malo momalimbana ndi amene akumaba makhwala zipatalamu mukalimbana ndizithu zoti simupindula kalikose palibe atakuyamikileni, musaiwale mr zakeyu kumalawi amamusowesa munthu wamakani musowa ngati mene anasowela chasowa .muzuzisa anaanu akakhala akazi anu zakwatila ndine

Jaki
Jaki
8 years ago

jce yomwe ukunyadirayo unaipeza cause makolo ako amalima fodya waiwala? upepetse mw depends on agric especially fodya.so who r u ungopempha anthu akuthandiza utaniutani ife ndi mapale. usadzaonere BB .iwe ndi mdani wa malawi

stevie phiri
stevie phiri
8 years ago

koma monga tose amalawi pangofunika kukambilana bwino bwino cus matimu opanda sposa ndizimeneso ikumabwezeresa mpila kumbuyo ziko muno ndiye pakufunika kukhala pasi ndikukambilana kusiyana ndikumangottukwanana

Asibu mlenga
Asibu mlenga
8 years ago

Or titabwera kwanu kuzaola katundu sangakwane kupangira sponser mbuzi

Styson longwe
8 years ago

zakeyu chamba sunasiyebe kusuta eti masponsership onse aja amowa,fodya mmene amkapanga sponsor muja unali mmimba mwayi wako,usadel nkhawa tikubwelera kunyumba yako,fisi iwe zamanyibasi.

Geoffrey Dyson
Geoffrey Dyson
8 years ago

Iwe zakeyu ,watumidwa eti,FAM is sponsored by Carlsberg,Malawi is depending on tobacco.The best u can do is to give BB 800mita kuti uchotse nyasa wamva chimutu chongokula.

chipembere
chipembere
8 years ago

thats bull shit!!!!!!……kodi amenewa nthawi yomwe kunali Embassy trophy FIFA kunalibe……kukula mopusa kapena kutumidwa….ma advert andudu amanveka mmawailesi ndi makanenmawa samawaona ….osakatseketsanso ma radio stationiwo bwanji…..ndekuti Ntchisi…kasungu….Mchinji..ndi ma boma ena asiyenso kulima fodya…mapazi anu agalu inu mukufuna kutchuka kapena…mbuzi

ngongoliwa
ngongoliwa
8 years ago

Please neba do not make any mistake talking about Limbe Leaf supporting Nyerere. Those were old days when Tobacco money was not considered bloody money. Today there is global outcry over nicotines from tobacco. Curse to those who touch or use bloody money from tobacco. In fact I was surpised how possible that neba can source sponsorship of over 5 million mite. I knew it. That is bloody money.Drug fighter please separate these two aho wants to promote use of blood money.Head on Zakeyu.You are getting support from Nyerere Family. Hahahahahahahahahaha I am enjoying this world. Ndimkadabwa a Thewesa ayi… Read more »

mwana mulopwana
mwana mulopwana
8 years ago

Nelson Zakeyo , no surname but all first name, what does this man called Nelson Zakeyo smokes, I cant even deduce from his name his district of origin otherwise I could have done more investigation, useless man, if t all this man has a wife, it is better for the wife to seek divorce, this useless man will not assist the wife to grow, a man full of jealous, We need a very good bill in Malawi to be passed so that useless NGOs like this one should not find a room in a our beautiful country, it seems most… Read more »

Gadabwali
Gadabwali
8 years ago

Zinthu tinakambirana bwinobwino tapedza sponsor mukusokoneza. Ndiye iwe Zakeyu dziwa izi: Sikuti umakhala kumwamba ayi tili tonse. Tithana nawe nzeru ulibe. Wapangana ndi anzakowo mutisokonedze. Ife zokamba zambiri ayi. Tingobwera kunyumba kwako utipatse Sponsorship basi zokambirana palibe.

Read previous post:
CSOs brainstorm on govt failure to table Information bill

Civil society organisations are this Friday meeting to chat the way forward following government decision not to table the Access...

Close