Email a copy of 'Ex-Malawi president Joyce Banda reaction to Lutepo's cashgate claims: Full text' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

46 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Bornface Awali
9 years ago

Amayi ananena kale kuti Odi uko amayi aduse osawapingapinga mukapitiliza mizimu(Amazozi)akuzuzani musowa mtendele mukulimbana ndi muthu amene wanthandiza athu ochuluka ziko muno muzingoyendesa boma lanu lobela tikanafuna tikanakusiyani kuja chifukwa munabela zikolino limayenda bwino pamene amalamula amayi mu chipani cha PP,Osamawapaka manyi Amayi .Yao culture heritage arts Bornface awali!

Manjolo
Manjolo
9 years ago

Mrs. Joyce. Banda. Don’t say anything. Wait and see which way the cat jumps.

ACHEDYIKA
ACHEDYIKA
9 years ago

mukulimbana ndi mayi mavuto anu ndichani osapanga zinthu zoti zikuthandizeni

Imraan Sadick عمران صادق

We understand that of late anything that comes out of Lutepo’s mouth can’t be taken seriously since he has been changing statements like underwear,however,
that does not mean his testimony is going to be ignored completely because there’s (call logs)(CCCtv footage to assent to ,hence don’t get too comfortable
I for one as a citizen of this country, I am certain there’s no way Mr Lutepo could manage to siphon such huge amount of taxpayers money single-handedly without big fish’s involvement

Dyomba
Dyomba
9 years ago

A x presdent asafulumile kuyakha iwo sanaitanidwe kukhothi,asiye omwe ukufunsidwa aziyankhula adya mulumila thawi yawo ikwana azalongosola bwino.

wanted
wanted
9 years ago

Tisaopsezanepo apa

Bwitoto
Bwitoto
9 years ago

Kodi inu bwanji mukulimbana ndi munthu wa mayi? Mulibe chochita eti?. akanakhala kuti JB alibe ndalama kodi nanchidwe wanu uja Bingu akanamusankha kukhala his running mate? Kodi inu kunalibe? Bwanji amaleka kusankha bwampini wanuyi? Zopusa eti. Mumuuze Atupeleyo kumene aliko kuti makobiri aja mthumbamu mudakalibe!!!!! Komanso madzi mu mpope sakutuluka. Osati zanu zopusazo mxiew!!!!!!

Bantu
9 years ago

She should have consulted her legal advisors before exposing herself in this way.

Trust
Trust
9 years ago

Mai Banda must explain something about cashgate, where did she get all the riches within 2 years? As usual she is busy building her international reputation at the expense of Malawian. JB come home and lets build our country osamangodya ndalama kunjako

Nzeru za akulu
9 years ago

Lamulo lisatidwepo apa and atolankhani you are not judges pliz zisiyeni mmanja mwa court zogamulazo

Read previous post:
Lutepo implicates JB, accepts cashgate wrongdoing on radio: Bows to Malawi govt pressure

Cashgate scandal that has seen billions of kwacha looted at Capital Hill at the expense of the general populace has...

Close