Email a copy of 'Exposed! Walter wants to bribe Police for FA Malawi polls' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Exposed! Walter wants to bribe Police for FA Malawi polls' to a friend
A Malawi College of Accountancy lecturer, Dr. Auxius Kazombo Mwale was on Sunday arrested by Fiscal and Fraud Police Unit (FFU)...
Nthawi ya kampeni ndiye yoteroyo. Aliyense amakhala wadyako,inuyo mwadya from different camp or you want Nyamilandu’s attention zimenzo amene timadziwa campaign is not news, for it is for the writter’s benefit, mwaitenga boo, “Let the richest camp win!”
patsani mpata achinyamata palibe wamuyaya. no to third term -chiyambiri kutsata mpira kumangomva Nyamilandu we need change…
walter ndimzika ngati m`mene alili enawo, ichi ndichisankho aliye amapanga campain kuti awine ndipo amayenera kupanga chilichose kuti agojetse azake. Tsono ngati enawo akungougona asiyeni abapha mkononowo, walter akuchita zija amati fumbi ndiwe mwini.
Nanunso a secret reporter, anzanu akafuna zoterozo amaika phone ku silent. Inu chi volume wooo pamene mumafuna mumve mwakabisira. Lack of vision! Osanamapotu apa.
Why is Nyasatimes wasting their energy? I am not a fan of anybody going to the FAM polls but I can smell something sinister about this whole Walter saga. Last week you came up with the match fixing issue of FAM and Nigerian FA accusing the incumbent of heavy involvement. Now you are at this. I don’t know whom you are campaigning for in all this because as it stands even you yourselves know that there is no credible candidate worth his salt apart from Walter .I really do not see how Walter can be booted out. The whole set… Read more »
a madzi, we started hearing your horse voice long time ago…we dont like u Fool….Umaona ngati wanzeru ndiwe wekha, stupid….idiot stop clinging to power, mbuzi
Hahahaha! room 216.
Mwayamba kale , Mwayamba kale, Mwayamba kale kunjenjenjemela, mutangongova kuti Walter akuyimba #singing#
nyamilandu wayamba ufiti……poor malawi
atolakhani aku mw,kumulonda mzanu paka ku room yake.mayesa Nyirenda&mwenda ose ndi aku FAM muziona cholemba