Email a copy of 'Fake Malawi Police recruiting officer nabbed' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fake Malawi Police recruiting officer nabbed' to a friend
In 2001 Malawi’s commercial capital, Blantyre was named the world's most desirable habitation and today the new Mayor, Noel Chalamanda...
Shame my fellow malawians zuto ndi lack of jobs in our government
Achewa achewa bwanji tapitani kwathu kumpoto ku u tenant once instead of kunamidza anthu
Imeneyo ndi treason. Nanunso ochewa kupusa koteleku bwanji? Mukamavala makanja tinkayesa muli ndi nzeru pang’ono. Mpaka kubetsa certificate? Mbatama zezenizeni.
Wakuba ameneyu.
Wina ku 30 komweko is demanding 30 pin per head to attend interviews yet anadya kale Dollar zina kuti mayina atuluke pa list. Koma nde mulemera..
tsanotu yapapa niluwona kuti omalakwitsa niyawa okubomawa,mainifolomu yena yapolisi yamafanana ni ovima beni moti wanthu okumudzi sosiyanitsa wapolisi ni ovina ben
Ndepanyasaland pamenepo
Chinyengo komanso kusowa chilungamo ndiye vuto kwa onse.
Had it been that I am a Policeman, I would have charged both the man & men knowingly breaking the law.
Koma anaganiza bwanji ? munthu ameneyu ofunika akagwire nthito ya kalavula gaga chifukwa wayipitsira mbiri a Polisi.
kkkk. koma anaiwerenga. hvy