Email a copy of 'Father of David Banda praise Madonna: Yohane pleased with Malawi visit for son' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Father of David Banda praise Madonna: Yohane pleased with Malawi visit for son' to a friend
Giddes Chalamanda last week fulfilled his dream of performing in America but returned home on Wednesday through Chileka Internationak Airport...
Mwana wakongola uyu. Better to have a living, educated, rich son living in USA than a malnourished, impoverished, illiterate stupid son living with you in the same house. Champweteka aphulike. Mabungwe manyazi bwaaaa????????? Inu mudzingomenyera ufulu wamathanyula basi mpakana imfa. shupiti wanu nonse
Kkkkkkkkk. Koma ya. Ali wakhanda munalephera kuchitapo kanthu ngakhale boma lanulo linalephera and limalephera kuthandiza Ana amasiye lero wakula mukufuna muoneke anzeru?
A yohane Banda musatinyenge. Zikangothatha mthumba ndalama akupatsazo muyambanso kusokosera
Kubwera kwa Madona kwachititsa anthu ena kuvala zovala zosita bwinobwino. Inde inu yathu ija!
Kununkha a Malawi muzisamba ndikuchapa nkamwa
Any wise and intelligent child will look for his/her biological father or mother when he/she grows up. Blood is thicker than water. Well done David, well done Madona
Nayeso wadya banzi ameneyo amutseka pakamwa
Hahahahahaha olo asadye banzi, what can he do. He failed to take care of the young boy, nde pano uti wadya banzi? Umafuna azilalata zopusa ngati angamusamare mwana. Kenako amutenge, abwere azafe ndiumphawi nsanje bwanje….banzi or no banzi David is better placed where he is.. Chamba eti
Life is interesting!!! The so called Yohane who earns 50 pounds a year now has four more children???