Email a copy of 'First Lady awarded degree from University of Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'First Lady awarded degree from University of Malawi' to a friend
Malawi Parliament has been urged by civil society organisations to reject the adulterated Access to Information Bill (ATI) when government tables...
Malawians why are we obsessed with being accorded with doctorates or awarding doctorates osalowera mkalasi. Serious? For sweeping the street lol. Those receiving honorary phds must prove it academically. Awa angalembe thesis. We shall never develop with a bunch of Drs’ opanda academic achievements
Congratulation mai wa fuko
Just a correction to the reported perception of Beam office. An Honorary degree is not an academic degree. Ndi ulemu wongoyeseza. The recepient salowela mkalasi ayi. Amangovala mkhanjowo osagwilira ntchito ya mabuku mkalasi ayi. Indeed some recipients prefer to not call themselves doctors because in reality they are not doctors.
ok
YOU CAN ALSO DISCUSS THIS IN AUGUST HOUSE
NO WONDER WE REMAIN BEHIND. ALIYENSE AKAKHALA PA MPANDO KU MALAWI AMAFUNA U DOKOTALA BASI. COPYRIGHT SIMUMACHITA NAYO MANYAZI.
KU MALAWI BESIDE KAMUZU KOMA MULUZI DR. MUTHALI DR. JOYCE DR. UYU WAGANIZA ZOMPATSA MKAZAKE UDOKOTALA WOTOLA.
KU TZ. KULIBE ZOPUSAZI. KU Z KULIBE KU ZIM KULIBE KU MOZAMBIQUE KULIBE. AMALAWI KUKULA MTIMA. MCHIFUKWA POLY INASANDUKA MSANZA ZA UNIVERSITY.
ma DR a fake, wachitapo chni kuti akalandire Doctorate,
za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii?
what a stupid thing! sono mwapangapo chani? Nonse ndinu a zweeee eti?
what a stupid and time waisting activity. ndiye chani chimenechi???
Ofumu okakhala udyo simouza, imouza ndi mphepo!