Email a copy of 'First Lady behind firing of State House staff' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

86 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mayazi
9 years ago

she is stupid . She has to know that shes not there for long,she is not even in the civil service and she has no such consitutional powers of firing the state house staff. Can the president stop this please!

Maliseni
Maliseni
9 years ago

I am surprised with these claims ife anthu aku Balaka sitimada anthu, ndife okonda kukondana. Ndibwino kumanena zowona, otherwise ma agents odana ndi amami mulipo ambiri, tikuingani ndiye ife tikadzazana ku state house mukapitiliza.

Patriot
Patriot
9 years ago

Wakuba akaberedwa amamva kuwawa kaya chifukwa chiyani kaya?

Nabanda
Nabanda
9 years ago

Abale Getrude Muthalika kukalamba ngati sali ku State House. Is she being mistreated?

empty tin of nyika republic

I knew kuti walemba izi ndi mtumbuka. Nzeru njee! Koma kukula kukamwa basi. Anthu inu mayeso mumakhonzeradi kuwonera eti! Paja kukaya ma invijileta safikako.

Yankho Lako
Yankho Lako
9 years ago

Bwanji osamfunsa Peter Mkhito ngati walemba ndi ka nkazi kake kaja ka chitumuka. Kapena ndi nkazi mtuumbuka wa Ken Kandodo walemabayo. Kapenanso ndi nkazi mtumbuka waFriday Jumbe. Zikhoza kutheka kuti ndi ana a chitumbuka a Bright Msaka amene alemba. Yeseranso kunena zopusa zakozo ndizakupitilizile mndandawu. Nincompomp

mtichimwitsa
mtichimwitsa
9 years ago

Zaziiii

Political Analyst
Political Analyst
9 years ago

It might be news to small gossipy minds.Otherwise “No substance here”.Rather its personal.

Chikankheni
Chikankheni
9 years ago

This is not an issue I mean really! Can’t u try to get good news wit senses, when we open this site we expect to hear stories from home since some of us we not within da country, ndiye nkhani izikhala imeneyi abale, one day u.gonna tell us dat amayi akuti akuti athamangitsidwa ku chikwati chifukwa anaphika nsima yosaphya….kkkk

Njalankamwa
Njalankamwa
9 years ago

Anthu ochepa matupi ndi choncho, madam gateee the sermon at JZU wife shld teach u a lesson! Tiyeni tizikondana. Moses Stephano is a great pastry chef! Mapwiya loved him, ngakhale mama Joyce. Ukanalawa ntvhito ya manja ake! Mmmmm shupiti. Muzakusiya nanu nzosiyilana. Mufuna kudzadze BLK

prescilla
9 years ago

Musatinyase ife aziiionah

Read previous post:
Malawi to sell controlling stakes in Indebank, MSB

Malawi is selling portions of two commercial banks to re-capitalise in a move meant to turn around the struggling banks,...

Close