Email a copy of 'First Lady cheers Neno fire victims, donates relief items: Appeals for more support' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'First Lady cheers Neno fire victims, donates relief items: Appeals for more support' to a friend
Police in Nkhotakota are keeping in custody Peter Mambiya who surrendered himself to the police after he killed Gibson Mwale...
With compliments to NAC. Kodi misewu musesa liti ?
Kuputsisa Amalawi. Nanga ngozi inachitika ndi liti? Ngati ndinu okhuzidwa bwanji simutume ma adviser anu msanga kuti akawapepetse anthuwa on ur bhaf? OSAMAWATSEWERETSA AMALAWI CHIFUKWA CHOTI NDI OTSAUKA.
NAC????
Nanu mwayamba ma hand outs. I thought your “husband” said there would be no handouts with this administration??? Mulomowu mulomowu mulomowu mulomowu udzakupeza
Koma anthu ena eeeh sadzatheka. Nanga apa pali nkhani yoti wina ndikulalatanso apa? Kungobadwa oola mkamwa basi? Winawu ndi umbuli womvetsa chisoni ndithu. Ngakhale polemba mumabisa maina anu komabe mwainu uzimu udzikhalamo
good gesture!
Kodi ndalama za NAC zija anabweza?
Mama first lady, uku ndiye kukhala ndipo osalema pa kuchita zabwino. God bless
Koma abale tayamikilani amzanutu akachita zabwino Ngati izi.
President sent his wife to condole on his behalf? You malawian please stop making babies because you don’t have a decent president with sympathy among you all my fellow malawians. God bless malawi no matter what the idiots may do.