Email a copy of 'First Lady to champion family planning intiatives in Malawi' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
sad
sad
8 years ago

koma make up mwaonjeza. less is moreeeeeee.

JENTTELE
JENTTELE
8 years ago

PAJA MAYI WATHU ABITI GETRUDE MUTHARIKA MUKULERANSO , AUZENI AZIKAZI ATHU KUTI ANBVETSETSE CHIFUKWA ENA NDIAMAKHANI KWAMBIRI .
KOMANSO MUKUKONGOLA BWANJI , KUMUTHU KOKAKO NGATI ” PEACOCK “

ganganinga andy
8 years ago

Gud idea koma osamayamba zinthu kuti mzitukule nokha iyayi thandiZani ena as a first lady

mtima wa nyani
mtima wa nyani
8 years ago

pa dzana kodi tikukumbukila HEALTH FOR – 2020???????????????????????????
mpomwe acina gudo gondwe ndi gulu lao anakawa dzindalama koma nde kunali ma truck kugulidwa nthawi imene ija . nde mmene HIV , CHILD AND MATERNAL MOTALITY MMENE YANYANYILAMU- ARE U SURE U WANT TO DO SOMETHING NOW.CHANGE THE RATE WE R DYING OR CONE US IN THE NAME OFCHANGING THINGS? KUKAMWA NGATI MPHUTA TATOPA NAUNU. NAC YUYENDA BWANJI, NANGA KUSESA MMISEU, DO WE SEE ANY CHANGE SINCE- THINK TANK PLS. NDANGUDUTSA

mtima wa nyani
mtima wa nyani
8 years ago

kodi mmesa za umoyo wa azimai zinayamba kale???????????????? bwanji osangopitiliza mmalo mopinda dzina kuti mupeze zoomba zina ndlama agalu inu. koma a mw nde sitikuganiza. nde mukacoka wina adzaikeposo dzina lina podyela. are u looking into the womens health, mwacitika ucitsilu tsaano. you r swindling our minds for the sake of corrupitng our taxes.

Hehehede
Hehehede
8 years ago

Mwayambanso safemotherhood mwamwatani?

safusa
safusa
8 years ago

Kusowa copangatu uku. Tangokhalani chete and do whatever it is you do in Sanjika or wherever|

John
John
8 years ago

THIS IS THE MOST SENSIBLE THING I HAVE HEARD FROM DPP GOVT. FAMILY PLANNING. IT IS LONG OVERDUE. JOYCE BANDA SHOULD HAVE BEEN CHAMPIONING THIS WHEN SHE WAS PRESIDENT. BUT ALAS! HER SELF-MOTHERHOOD WAS UNDERSTOOD TO MEAN ANTHU TIZINGOBEREKANA MWACHISAWAWA!

Namaoda
Namaoda
8 years ago

Anadimba kodi ndinu a miss matofotofo. Aliponso akonda anzanu ochepa matupi. Enanso akonda matofotofowo.

Mgoloso
Mgoloso
8 years ago

Akulu mwasiyatu mfundo apa,,,,,bwanji osangokhala?tiyeni tizikhala serious pochita zinthu,,,,,,iyi ndi nkhani yabwino koma kumainong’anso

Read previous post:
Blakjak and Gwamba drop a surprise single ‘Mwam’puta Dala’

Blakjak has resurfaced with another 2015 single, a dancehall fusion Mwam'puta Dala featuring the hip-hop voice of Gwamba. The song...

Close