Email a copy of 'First Lady to crown Miss Lilongwe: ‘Beautify Malawi'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
shaaaa
shaaaa
9 years ago

atumbuka aku lilongwe amenewo.umadziwira nkhope zofanana kuyera koma mitendo yokuda.fanta n coke koma kumeneko gondolosi pambali,timisinkhu tofanana kukalamba
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

passwell
9 years ago

a first lady ndiati apa? awina chifukwa chanji? majaji amasankhila mantha kapena chani.peter munthalikayo nkaziyo omufunsilila kapena bwanji? zosafunsaso apo coz amati zonse mudzina la munthalika ndizotheka.mayi president kuwonetsa mbali mwa bwete ku gulu? ayi nzachilendo.zinakambi zina leku ku Lilongwe kuli ma baby owoneka bwino osati ma baby akatumba ofufuma ndimapili a mu ndilande ndi mbayani.kikikikikiki mukawona ma baby a pa poly owoneka bwino akuchokela mu Lz.

ghu jumpyo
ghu jumpyo
9 years ago

Koma zina inu..!!

SAPITWA
SAPITWA
9 years ago

NKHWANGWA ZOKHAZOKHA PALIBEPO OKONGOLA APA.

fkr
fkr
9 years ago

you call these girls the most beautiful oh the country. please is this a joke.Gertrude please stop wasting tax prayers money on this crap and start doing something positive to really beautiful Malawi. clean up the garbage that litters the town’s and roads. fix the broken street signs, paint the buildings. etc. is not difficult to do.

Khuth'upa o'Machemba
Khuth'upa o'Machemba
9 years ago

Koma ma style a kaimidwe asikana a ku Lilongwe’ko amaphunnzira kuti? Kodi achewa inu: are these your best models? If so, ndiye muli pa mavuto, zedi. Mitundu ina yonse mziko lino lapasi, imakuposanitu apa. Ngakhale nkhopeso, “hair style”, zovala olo ma smile a mchire eeeeh, achewa!

A Molotoni
A Molotoni
9 years ago

Atsikana okongola awa, ngati mwafa maso zanu zimenezo, kaguleni mazenera. Imeneyi ndi sample yaku Lilongwe. Kungoti chabe sangafanane ndi olo ogulitsa ma units aku Blantyre. Kuno timanjoya guys, ma babe okhawo ndi nyatwa, inuyo kungobwera, mudzidzayenda otota n’town, bola musadzagwililire ma baby athu.

Puludzu
Puludzu
9 years ago

Ndikuonapo mkazi okongola apa ha ha ha akazi onse tilinawo mu L city wa awa achokeranso kuti?

Walira
Walira
9 years ago

Ndi zizukulu za Getu kodi zikupikisanazo? Timatupi ta malnutrition ngati Getu amene. Adyetseni kaye sibusiso for six weeks ndiye muzapangise gule ameneyu. O Geturudi nanu mutha kumadya ndi kukapanga nawo compete.

kate
kate
9 years ago

Kodi beautify Malawi na beauty contest vikuyana waka? za ziiiiiiiiii

Read previous post:
Zicco Mkanda net brace in Mozambique

Mozambique-based professional Zicco Mkanda has started from where he stopped last season after scoring a double to inspire his tea...

Close