Email a copy of 'First Merchant Bank robbery prime suspect Malunga dies' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

51 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mnyamata oyikonda nyasatimes

ku TZ akagwira mbava kwake kwatha thus umbava ndiochepa kwa anzathu. ku malawi apolisi kumwa bawa ndi mbava kenako hire mfuti kuti mbavazo zikabere. mulungu ngwamayankhi adzayankha

Gibo
Gibo
8 years ago

Big up police anthu amenewa afebasi

MALEPA
8 years ago

Mbava zoipa ndi a policewa amalawi,mfuti amatenga ndiwo kupangitsa hire kwa mbavazi,boma lionetsetse genesis wa umbava nchifukwa amwapanga bail mwachangu,Pelekani mesa ankangoyenda thimalirizii;”akazi anga ndi bwana ku BLATYRE POLICE”,banja linatherakuti? Mwapereka umboni? Mulunguwathu salolnso kuti munjoye ife misozi ilimbwembwembwe m’maso,MALAWI UNALI WABWINO KAMUZU ALIPO IWE!!

apundi says
apundi says
8 years ago

eya ntchito ilipo ku jehenako, mukaona kuti Jesus ndi dolo RIP

kanyimbi
kanyimbi
8 years ago

They should not die before revealing their friends and bosses. Why are they dying before taken to court? A Polisi pano ndiye mwawonjeza. We are suffering yet the real robbers are these men in uniform. You steal from the roads during the day and with guns during the night.

wamuona satana
8 years ago

We would have loved to see his photo…

amfana
8 years ago

utenge ndi futi yako yomweyo aise pelekani malunga uzikabera kupaladaizo.

Tiwuzeni Bwino
Tiwuzeni Bwino
8 years ago

Anthuni musathamangile kusekelera kuti Malunga wafa. Kodi tinawuzidwa ngati ndalama anabazo zinayendesedwa bwanji. Malunga atamangidwa anawulala chiyai? Nkhaniyi ili ndi zibowo zambiri.

The captain
The captain
8 years ago

Perekani wapereka moyo wake mopusa… Umati chani pwanga each dog has its day. Six feet pwanga akumangirenso concrete kenako chipilala uziba kumanda komweko galu. Koma ndibwera kumaliro ako osadanda pwanga

Charombanthu
Charombanthu
8 years ago

Chilichonse chouluka tsiku lina chidzatera….

Read previous post:
TNM donates K6m to Malawi blood bank

Premier mobile service provider TNM today proudly announces the donation ofK6 million to Malawi Blood Transfusion Service (MBTS) to help...

Close