Email a copy of 'Fix bus, FAM orders Luso TV: Wanderers blame crazy jubilation to brreakdown' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fix bus, FAM orders Luso TV: Wanderers blame crazy jubilation to brreakdown' to a friend
Malawi Golden Boot award winner Richard Mbulu will not be able to join Mozambique club Costa da Sol as Mafco...
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk bola tinakukomolani a bullets mukuoneka mukumapanga comment mutakunga muscles kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk mvuuuuuuuuuuumu
Amene amayendetsa ndindani mayina awo.Kodi Ali ndi ma valid driving license ,komanso inu a FAM kodi nditabweretsa ka plasma 42″ zingatheke ka bonanza? Ndiwuzeni mwachangu chifukwa iyi ndi Samsung original
Akonze okha a Nomawo
Zovuta kumvetsa ndithu. Mwati oyendetsa anali ndani? Okonzetsanso akhale ndani?
You should see the bigger picture. Kkkkkk aMalawi alowa kuba tsopano. Luso TV made huge profits from gate takings at Bingu Stadium more than they spent to bring that old rotten chiphapha Nissan minibus. If the company that manned the gates made US$4,000 equivalent how much did Luso TV make? This bus will cost you around US$2,500 fair price in Japan. Iyi ndi Lusogate big time! FAM you are culpable in this thievery. You ought to vet some of these prizes before sanctioning such crowd pulling games. You are lowering football standards in the country. You are killing the game… Read more »
kkkkkkkkkkkkkkk
I think a FAM ndi amisala choti Luso Tv chakhuze pamenepa ndi chani pomwe amangoyendetsa aliyense.Kodi kapena inu a FAM mumasapota wanderers?Mumaikondela bwanji?Luso Tv ngati ikundimva asakonzese min bus imeneyo.Kuli bwino akakumane ku court akapezeke olakwa chilungamo chikaziwike.
no need for LUSO TV to pay for the garage services,anena kuti aliyense amangoyendetsa even yemwe si driver.
In short bus awononga wokha.
In all fairness, Wanderers should repair the bus because they simply damaged it by letting each and every player drive it. It’s stupid and ignorant on the part of management to allow such perilous activity to occur. Luso did their part, basi
Dats unfair to Luso TV coz awononga okha ma players a Noma Bus koma mukufuna Luso tv ikonze pali chilungamo? Tikamanena kuti Fam ndi ya Noma ndekuti tikulakwitsa?