Email a copy of 'Football Association of Malawi raise players allowances' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Football Association of Malawi raise players allowances' to a friend
The Center for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) and the Center for Development for the People (CEDEP) have urged the...
Take the resources and help the queens,thy put us on the map not makape mukuthandizawa
Allowance MK6 000 ONLY? Shame to my country. ife timadandaula akamatipatsa R250/day kuno. means timawaposa ndi Mk4 000? shame.
Uku ndiye kubetsa ndalama.
Dziko lathu ndilosala ku zambiri chifukwa cha umphawi koma kandalamaka kathandiza kusova timavuto tinantina kufikira Mulungu azatidalitse.Kuyetsetsa timayetsetsa sikufuna kwanthu koma mavuto achuluka nziko lathu.Ma players athu ziyetsesanibe kulimbikira kuti zinthu zizisitha pang’ono pang’ono.Ndimakunyadirani anyamata athu
Money is important motivator.Hope the adjustments will will boost Flames performance in the next games.Lets go guys!We can do it!
Good development may be we can see changes in the coming games
palibe chomwe akupanga mukungotaya ndalama za zi!!! Bola muzithandiza chipoloplo ya ku ZAMBIA
FAM mwayetsetsa zakanike okha