Email a copy of 'Football pundit Charles Nyirenda nicknames Kangunje as ‘Silencer’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

28 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
black
black
8 years ago

big up kankhunje. show them the ril futbol..

wanyerere ubooka mmimba

yesetsa mm’bale ulimbikilebe mwina tsiku lina maloto ako omenya chitimu chandalama cha nyasa bullets nkudzakwanilitsidwa

Kabaka mutesa
8 years ago

Ulemu wanu bwana Kangunje ntchito mudayigwira yotamandika

yemweuja wazisomo
yemweuja wazisomo
8 years ago

thats de development of football

zidana
zidana
8 years ago

Iwe kangunje malangizo anga ndi awa munthu ukafikapo ndipamene uyenera kuganiza mofatsa cos ma team ambiri amakufuna ndiye ukatengeka udzapanga regret, iweyo pitiliza kumenyera civo kudekha ndikwabwino umadzasimba lokoma anzanu anadekha a Willy Chambwinja pano akuyendera magalimota opuma chifukwa anadekha osapita team ili yonse atafikapo pano zabwinobwino

yazula
yazula
8 years ago

Mzimba Solola ufune usafune Nelson ndi silencer basi he silenced the nomads family,ndiye ndingokukumbutsanso kuti bcz of the gud job he does upon wandalazi,panopa ndi NELSON SILENCER KANGUNJE, ngati uli ndi zifukwa zina ask KANGUNJE yo nde poti anakupanga kale silence i dont knw kuti ukayambira pati mxiiiiii! NYASA BIG BULLETS MOTO KUTI BUUUUUUUU!

Dausi Phiri
Dausi Phiri
8 years ago

Kangunje nkachilombodi eti a neba mpaka kulira nazo zomwezi?

DOBO
DOBO
8 years ago

Chimene ndinachiona ine ku Malawi ndichakuti masapota ambiri a mpira ndi masaveji.Nyerendayo amapereka maganizo ake ndipo palbe chiifukwa chomunyozera.Usapota wa usavaji basi.

Mulhupalhe
8 years ago

Let kangunje B kangunje if else enan muona….

chakuda
8 years ago

Ndale ndii mu mpila momwe!!!!!!!!!

Read previous post:
MP Mkandawire attacks deputy speakers on illegal allowances

Outspoken Mzimba West MP Harry Mkandawire systematically hijacked debate on the State of the Nation Address to demand an explanation...

Close