Email a copy of 'Fracas in Mangochi: Malawi police clash with community' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fracas in Mangochi: Malawi police clash with community' to a friend
American music group, Dru Hil was forced to cancel its Malawi concert after the organizers, Peermont Hotel managers of Umodzi...
Anthu aku Namwera atopa ndi khalidwe lakuba lomwe likaunikidwa titha kunena kuti ndi omwewo akusongolera. Ziphuphu too much! Kulibe chilungamo ku Namwera, chomwe amadziwa ndi kuwopsyeza basi. Tatopa ndikuopsyezedwa! Bwanji akawone zina. Kodi mafupa aja anawotchedwadi? Zovuta
Anthu anatayachikhulupililo ndipolice
Dats Mangochi i know siyifuna zachibwana, umbava wagona ku polisi
Imeneyo ndiye Mangochi,zachibwana sizimaloledwa. Ndi Bork haram area. More fire asamazolowere zachibwana.Our Mangochi,Our pride.
That’s Syria in Malawi. Life is not valued at that part of Malawi.
Anthu Anasiya Kukhulupiliro Apolice masiku ano because most of them are involved in the bad Act.