Email a copy of 'Fresh probe on Malawi Electoral Commission to start: AG says team to investigate financial abuse' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Fresh probe on Malawi Electoral Commission to start: AG says team to investigate financial abuse' to a friend
The High Court in Blantyre on Thursday adjourned a judicial review of a case where public tax collector Malawi Revenue...
I see atleast humanity in this stealing at MEC,they has been in this nation worse cases of theft and cash gate. Focusing so much on them will delay the worsed cases. A kalonga awo muwasiye a gwire nchito yawo. A mbendera wo ndimunthu wabwino kwambiri zikavuta amalira.
He already cried asking for GOD mess.
Kodi inu A Malawi kapena kuti maNYASA muli ndi ufiti oro tiziti chiani?????kuba kumeneku bwanji????????????
Palibe nkhani apa! Iwo ndiye akanatani ngati ma bwana akusosola $20 million ya asilikali? K1.3 billion ya ngongole ya Sterling ku MSB! K1.6 billion ya ma MSB toxins loans! K400 million ya World Bank……………………………………………………………………………………………………………………………! etc etc
Malawi woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee!!! Boma ilooooooooooooooooooooooooooooo!!
Tsoka mtunda ndi Nyanja ya Malawi pakuti wopipayo watskira komweko!!!. Dzikoli wolamumulira wake ndi Satana ndipo onsewa mukutchula ndi amitenga ake. Pakuti iye ntchito yake ndikupha, kuba, bodza ndikuononga.