Email a copy of 'From 'Ziphwisi' law, trust Malawi Minister Chaponda to say ridiculous things' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'From 'Ziphwisi' law, trust Malawi Minister Chaponda to say ridiculous things' to a friend
Malawi Congress Party (MCP) continue to gain more ground and attract more members with the latest being former cabinet minister...
As citizens of Malawi, we are supposed to know how our taxes are being spent. It is therefore unfair for George Chaponda to tell the journalist that he was wasting time.
Dr Chaponda amaoneka ngati sa samba kapena ku samba mankhwala
Don’t worry malawians God sees beyond the sea angatizuze bwanji koma one day is one day adzazisiya basi ngati m`bale wake uja
He realy fatted here,had he known how tough life of a malawian thobwa seller is,he wouldnt spoke it.
Mbuzi za anthu mukafika 2019 muli ndi mwayi.
Koseko ndkulephera
Musadandaule achimwene, ineyo ndamene ndalakwitsa, zonse adziwa n’mulungu. Munditumizire account number yanu, ndugawireniko kangachepe.
Enanu mwati dzana lanu ndinu a Matako a Pusi? Ndiye mwati tidzipatsana ulemu? Lanulo ndi dzana la munthu woti angalangize anthu kuti tidzipatsana ulemu? Ingokhalani chete.
Zonse zomwe mwanena ndamva, vuto si ine ayi koma nkhope yangayi.
Muzingovutika ine ndikudya ndalama zanu m’bomamu. Kukhala minister simaseweratu, kuteroko umphawi ndi omwe ukukubwebwetetsani. Ine ndiye wakubayo. Kodi nkhope yangayi siimakuopsani? Dikirani kaye, ndimayenda nditatsinzinatu ine?
Dziko lotembeleredwa lino. Kumangosankha atsogoleri opanda chidwi ndi mabvuto a dziko lomwe akulamula.
Truly, the minister should appreciate that playing the smart card guy will not bring back donors.