Email a copy of 'Gaba happy to fight for Celtic place' to a friend * Required Field Your Name: * Your E-Mail: * Your Remark: Friend's Name: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Friend's E-Mail: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Image Verification: * Loading ... Sharing is caring! 0 shares Share Tweet Pin LinkedIn Email Print
gaba!!ndi deal usachoke Ku Celtic kuopakut ungadzapange za chiukepo,matimu akulu akulu angat kaiza! amalamulibwa. ndi masapota ngat bullets kuno ndiye ngat sukuchinya zigoli ukakhala dani wamasapo then u will be fired.
Gabaaaaaaaaa
wawuka kwakufa koma usthe mawu kuti sungachokeko chifukwa zilibwino ukanyeledwanso uzachokako
Gaba ndi deal.More fire
Gud lucky
Gaba ndi deal .Zabwino zonse man
Ankhaza amati Gaba watha koma zaululuka zokha. Siife koma “coach”. Mockers be quiet.
woow! thats great Gaba big up .
Umakwana Gaba! Kuno unali mankhwala ophela nyelele!!!!!!!!!!! nde uko eeeeee………
WELL DONE GABA UMANGODZIWILATU.