Email a copy of 'Garrulous Chief Lundu calls Goal Malawi organisation ‘stupid’, bans it in Chikwawa' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Garrulous Chief Lundu calls Goal Malawi organisation ‘stupid’, bans it in Chikwawa' to a friend
The ruling Democratic Progressive Party (DPP) on Sunday welcome into its fold six politicians in Lowe Shire who have defected...
Lundu chitsiru ndi iweyo as you talk as if you have no head. Sukuluyi inakudutsani pati? Mukufuna kudya nawo zakuba eti? What if World Vision Malawi says no with your arrogance? Ndiwe dyabulosi Lundu mwana Nsena
Mfumu yadyera iyi.Is he different rom my chief, Kyungu ?Stupid !
Congratulations Paramount Lundu. Sibwino kumangoonelera anthu anu akuzunzidwa chifukwa cha chimanga.
Ndi a Kongilesi okha omwe amalolera kuti a Kaliwo, a Msowoya, a Kabwira ndi ena otero azizunzidwa ndi Chakwera mkumadikira kuti khoti lilowelerepo.
Stupid chief,ignorance is indeed equal to death.
With such type of chiefs Malawi can not develop. Words used by some of our chiefs are very unfortunate. You need to change our chiefs especially Lundu and Kyungu.
Congratulations Paramount Lundu. Sibwino kumangoonelera anthu anu akuzunzidwa chifukwa cha chimanga. Ndi Kongilesi yokha imene imangoonelera Kaliwo, Msowoya ndi ena otero akuzunzidwa ndi Kongilesi Mpaka khoti kulowelerapo.
I wonder where our chiefs are going? A couple of days ago it was Mwankhunikira, Kyungu and now Lundu. Ndalama koma ndalama. Nthawi idzanena posachedwapa. Continue losing your authority in cheap manner.
Ndimapasa ulemu ma fumu awa: Mbelwa Mzimba, Bvumbwe ku Thyolo, Chikulamayembe ku Rumphi, Kachindamoto ku Dedza, Nkosi ya ma kosi Gomanani , Senior Chief Symon ku Neno, TA Chamba ku Machinga, Mkhumba ku Mulanje ndi ena.
Mafumu ukamakumana nawo kunyadira. Ambuye akudaliseni mafumu aulemu oyimira anthu. Lets not politics dent you.
We just have to abolish izi za mafumuzi. We are not a kingdom and these fools are very retrogressive.
Most of the times when i’m listening to the statements or arguements that these people we call leaders including the president himself in Malawi make; i wonder if these useless people really deserve to be called ” LEADERS”. When they decided to run for whatever position they are holding, didn’t they say ” vote for me because I’ve got a solution to the problems you’re facing?” Or did they say ” vote for me so that you or the opposition will help me to sort-out your problems?” Why our so called leaders are so stupid or take us for fools… Read more »
Mr President clapping hands for the headless chief. A failed chief indeed, it thats the way of solving issues then pipo in his area have no chief. If at all there are issues, one would expect the chief to amicably resolve them and the whole DPP then encourages him.