Email a copy of 'Gerald Phiri resigns as Wanderers coach after poor run of results' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Gerald Phiri resigns as Wanderers coach after poor run of results' to a friend
Malawi Electoral Commission (MEC) chairperson Justice Maxon Mbendera has courted fire to himself over his remarks that he had pressure...
timu yatha basi manoma mpaka ndi karonga kukuchinyani koma musova chaka chino kochi naye wayalula mphasa zamanyazi.
neba makani wazionatu karonga uyisovenge
Kodi noma simungangoyamba bawo bwanji mpira ndiye wakukanikani—-a Yasini ndiye ndiolephera kale mwachosa kangati???….
Gerald phiri si coach osazitha ai koma vuto ndimaplayer athu kuzifila aiwala kuti amadya cpender evry amoth coach samachinya zigoli iye kwake ndikupeleka phuziro kwa ana ake monga momwe apangila mphuzitsi ana mayeso amalemba okha we thack mr phiri 4 good job zatikanhka tokha.
Nomads, my team.
Gerald, just because your fathers teaches at a school you think you can teach a football team? Mwaonutu mpaka Karonga federation yakuchinyani. KKKK
when misfortune persist even your dog can bite
Zikundiwawa kwambilii!ndizalila mpaka litiiiiii
Yatha noma basi
Koma mutha ma couch