Email a copy of 'Gift Mkandawire sponsored Sulom AGM and lost VP post' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

15 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
PM
PM
9 years ago

Malawi is one but Malawians are not one.

Lutepo
Lutepo
9 years ago

Duduzi mwayowoya! Mwati ngakhale mchewa anakatuma galu iye osabwera kuti azapikisane, a mkandawire anakaluzabe? Kkkkiii, ndalama kumathandizila abale ndi makolo.

duduzi
9 years ago

A Mkandawire, ndinu Mtumbuka wanji takhala tikukuwuzani kuti paliponse pali Mtumbuka adani amakhala tho, sakukufunani ndipo sakutifuna mpang’ono pomwe. Tawonani nanga inu, mpaka anthu a ku basketball anayamba liti kukawina second highest office ku football ….anthu oti have never contributed anything in football…zomwe akudziwa ndi basket ndi bouncing, komanso ma “ring” basi….koma chifukwa choti ndi a Chewa basitu …..A Mkandawire,e,e,e,e,e…..tapangani invest in football ku North…..musayiwale kwanu…abale anu sadzakuyiwalani ayi …osati izi zomangokuDyerani nDARAMA IZI….AzingokuDyerani makopala anthuwa…….SINDIFE AMODZI ABambo Mkandawire,……..pulikiskani…asi mwawona sono..angokuDyeranipo Basi….apita….Mupulikenge baDada …….gezani kumaso sono……..remember Confucious…forsaking kinsmen is foolishness of the hifghest order, degree or magnitude. Mwati mutchuke ndi… Read more »

Namonde
9 years ago

Sulom was re-elected ………Anyway ndizowawa ndithu kuti a Gibo aluza atadyetsa dollar yochuluka, nanga contribution kuchita kuposa bungwe?

Kokotowa
Kokotowa
9 years ago

Kodi ndizoona ku mpiraku mumabako kwambiri eti? Mpaka sponsoring ndi more than two mita! Panya panu!

Big Supporter
9 years ago

A Gift Mukadawina Koma Ndi Botomani Ndili Lake Limene Lidakuluzitsani. Sorry Very Sorry

ngalonde mlumba
ngalonde mlumba
9 years ago

Lunga Alfred ..your passion for football will pay off. Can see your strides. Goodluck

Jango
Jango
9 years ago

Good move atumbuka akwanamo

akulu
akulu
9 years ago

He was talking as if he had already won the post. I listened to MIJ that day . This Idiot Malunga was underrating and looked down suleman . I felt bad coz u need to humble urself before any elections

dunwill
dunwill
9 years ago

We can
say that Gift is a true sportsman his contributions was made out of sympathy not to bribe voters go on Gift you’ll make it the other day

Read previous post:
Mzuzu households defecating in bush – Survey by Malawi Red Cross

A recent baseline survey conducted by Malawi Red Cross Society through Water, Sanitation and Hygiene (WASH) Project has revealed that...

Close