Email a copy of 'Goodall allocates K150 million to Assets Director's office' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
MNGONI
Guest

Umbava weniweni mpakana K150million? Ubwino wa ofesiyi nchiyani poti kuno ku Malawi mumangofuna kudziwa kuchuluka kwa chuma cha Pulezidenti akamalowa m’boma koma akamatuluka mulibe nazo ntchito. Komanso nchifukwa chiyani munalemba ntchito mlomwe pomwe pulezidenti ndi mlomwe?

Ngati pulezidenti ndi mlomwe, mu ofesiyi mudzikhala mchewa, mtumbuka, myawo or mtonga. Ngati pulezidenti ndi mchewa ndiye kuti mu ofesiyi mudzikhala mlomwe kapena mtumbuka etc
kuopa kukondera ndi kubisa info zinthu zikavuta ngati wadutsa muyeso.

Apa ndiye mwayamba cashgate inanso a dpp mwaona kuti IFMIS anatseka mazenera.

MLHAKHO
Guest

Inu mumati tikakudyereni kuti?

Mbuzi imadya pomwe aimangirira. Simunati mukanalira mpaka 2024 woooo.

Ndiponso K150m yachepa kwambiri koma ikanakhala K1bn bola.
DPPiiiiiiiiiiiiii

FreeTechAdvise
Guest
FreeTechAdvise

So he has 150 Million to chew! Can you please tell us his detailed JD?

Chalu Chamala
Guest
Chalu Chamala

Is K150 Not Enough For The Newly Established Directorate? Think Of The Budget Allocated To Education Secter? Zakuba Eetii Mwayambasooooooooooo?

Master
Guest
Master

Thats alot of money for just listing down how much welath top officials have?????? no no per year thats lots of cahs u have just made the tukula guy a millionare from the blues, shame!!!

Patriot
Guest
Patriot

Zokuba basi. K150 million of allowances basi mxii

Ida
Guest
Ida

What for? Kumeneko kuli ma employees angati? The whole Legal Aid Department has been allocated the same amount for both salaries and Ort. Shame on you.