Email a copy of 'Goodall says JB fertilizer loan programme was ill conceived: Malawi govt fails to recover K11b' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Goodall says JB fertilizer loan programme was ill conceived: Malawi govt fails to recover K11b' to a friend
Government has repatriated over 200 Malawians from South Africa and is expected to repatriate over 2000 as they are facing...
Fisi akagwa mbuna salankhula. Uladi Mussa anangokhala chete atamuwuza kuti amuwulura komwe watenga ndalama zogulira nyumba ku area 43.
This government has nothing to offer rather than wasting time and energy on mzimai inu ndi amuna tapangani zanzeru tiwone.
You are failing to collect funds because during 2014 TripatriteElectionsCampaigns you were telling people that they should not pay back the funds.Today whom are you blaming.CHOYIPA CHIMATSATAMWINI.MWAZIONA.Even the issue of donors withdrawing budget support its because you were taking the issue of CashGate as aCampagningtool.Now it ishiting you back.STOP TALKING ABOUT CASHGATE AS ATHNG CONTRIBUTING TO YOUR FAILURE TO DEVELOP MALAWI.
Iyi ndi locally cashgate, anthu wamba nawo adyapo, atayeni basi, 11billion zingafane ndi 557billion.
Kodi awa siaja anaba ndalama za feteleza???
simple mathematics just subtract it from 577 full stop
Ngongole sapeleka ma politians ayi. Imeneyo muiwale anthu sadzabweza. A PP amadziwa zimene amachita pa nkhani ya ngongole zimene boma lao liapereka monga ya njinga za moto.
Abwere JB adzanene mmene ngongole ya fetereza ikuyendera kapena inayendera kuti anthu asamabweze. nanunso okongolanu mudzibweza. Aboma musatenge loan ina mpaka ngongoleyi idzathe.
koma ngati Uladi Mussa anakhala chete! loo pali kanthu apa kkkk kulongolora!
Goodall is too old putting spanners in this years FISP programme if it fails he is solely to blame for this, upto now fertiliser not supplied on disagreement with suppliers on prices