Email a copy of 'Gwaladi out on bail: Malawi singer faces sex assault rap' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Gwaladi out on bail: Malawi singer faces sex assault rap' to a friend
President Professor Peter Mutharika Thursday assured American investors that the country will provide security to their business. Speaking at Kamuzu...
Mwanayu ndichibwenzi chake kungoti tsikulo sadamupase dola.mutayeni akakwerenso wadzaka 10.
isaaa!uchitsiru kumachita kuyaluka nawo choncho,ngati ndinu nokha anatokupatsani nthumbwana(maliseche) mkabudura ogonera ana aanthu,katofota kameneko mukayamba kudwala,simumatopita ku kch mukaone anzanu momwe atovutitsira achibale ndi matenda amgonagona.imfa ya munthu ochimwa Mulungu samatosangalala nayo.alomwee alomweeeeee!mapwiya makaka
Kodi nkaziyo amakataniko kuchipinda cha gwaladi. Khaniyo kumayiona bwino akuluakulu pls. Zogwilizana basi. Tangomuchajani gwaladi akapitilize luso lake loyimba kkkkkkk ati gwaladi ndiokongola dziko lose kkkkkkk uziona wakula watha. Cape town
Anyway tiona mmene zitathere
Koma anzathu a chewa mpaka akazi atatu munthu adakali mnyamata? Bola ife atumbuka tikumalera.
AYII ABALE AMAPANGA CHOOCHO?MAUDI AMALENGA MAN.LEROTU NDIIZOO WAZIMENYA DABOOKIKI.
Akuimbilani nyimbo muona
May God be with Gwaladi.
‘Ndikanadziwa sindikanapanga ee!Ndikanadziwa ndikuti sindikanachita ee!Lero ndagona mchitolokosi inee!Ena akuti ndi bodza,ena akuti ndi zoona!A khoti ndiwo adzagamule yee!………
Amkulu amalangizo wa asaaaa zimati iwo kupeleka malangizo abwino awa ntchito zapakamwa pawo zawachitira umboni ndikanadziwe eeeee sindikanapanga aaaaa nyimbo yake imeneyo kikikikikikikikiki……..