Email a copy of 'Gwamba to perform in Zimbabwe and Swaziland in April' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Gwamba to perform in Zimbabwe and Swaziland in April' to a friend
Malawians on Friday embraced the all-new Nissan Qashqai in style at a colourful ceremony in the commercial capital Blantyre where...
Zimayamba choncho kenako kumerika, ife kutmat analimesho wanga.
Zaziii.K
a gwamba ndikachaninso?
Big up Gwamba! thus what we want.
Mawu oyimbira ali nawo koma kulemba nyimbo satha e.g. from bola kusache song pena pake amati ‘ kamba ka deforestation tikusowa mtengo wogwira’ this gives no meaning, they hv different meanings. Osamangoika mawu for the sake of rhymes. This is jst an example from his songs. Nyimbo zake zambiri amakonda kuika mawu amene matanthauzo ndiosiyana kwambiri.
Well done gwamba for securing such project and all the best on ur tour. Thats what malawi music lovers are expecting to see and hear. Takufirani mr Gwambizo
stage work gwamba imavutirapo,not only him,oyimbaso ambiri akumalawi pastage zimavuta..Hope mukapanga control phuma mr as chris has said already.Nyc tour.
Amakuwa kwambiri when rapping and does not control his phuma when performing live.was not impressed with performance during kajive finals
Osakayimba chichewa man,,,compose english songs..
One One Kenako Ku America