Email a copy of 'Head of Malawi Catholic cautions Mutharika on ‘Ndidzakunyenyanyenyani’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mario wakumm'awa
mario wakumm'awa
5 years ago

Ambuye Msusa, r u serious that when the president said(ndizakunyeninyenyani) he meant violence?inu munakulira kuti? sukulu yanu munalekeza STD chiani? Don’t think that for being head of catholics here in malawi means everyone should dance ur tune no no no!!!!!!
If u want to support Chilima u r free to do so as a citizen of malawi not otherwise. If u like just come at the open and join politics as your friend chakwera did. usasokoneze anthu wamva!!!!

Low Learner
Low Learner
5 years ago

Inu anthu asambi kwambiri, zoona mungamuchosere mzanu kachulu ndikuikapo chi Mulanje Mountain. Mizimu ya Chilima will haunt you.

Systems THinker
Systems THinker
5 years ago

Msusa you know what exactly APM meant. Usakhale ngati siwe Mmalawi. We know that you need SKC. Supportani you are free koma osabisalira zopeperazo

MWENDATO
MWENDATO
5 years ago

WORDS SUCH AS ASIYENI APHATIKIZANE LIMIZO NDIZAWATHIBULILE LIMDZA AND NDAZAWANYENYA ARE WORDS WE HAVE BEEN USED TO DURING ATCHEYA AND BINGU. WHERE WAS HIS GRACE THOMAS MSUSA ALL THIS TIME. I DO REMEMBER I HAVE CARTONS DEPICTING THE KUNYENYA NYENYA WAR OF THEN 10 PRESIDENTIAL SAGA.. TO SAY THE TRUTH THE ROMAN CATHOLIC CLERGY ARE FIGHTING AND CANVASSING FOR SKC LIKE IT OR NOT. JEFFREY IS RIGHT, COME OUT IN THE OPEN

Dangerous DPP
5 years ago

Thank you for telling this old man. Kamuzu once used the same language and said those trying to challenge him would be meat for crocodiles. Though no one was fed to crocodiles all opposition thought it was true but that was the same political rhetoric used by Pitala. Bakili used to say atumiza ndege zopanda mapiko.

mkandawire
mkandawire
5 years ago

che-msusa you were quite on albinol. kapena u are one of them( dealers)

Hatton
Hatton
5 years ago

AROMAwa ndi afalitsi. Ali ndi ana mmalokeshonimu. Enawa mpaka majunior? Chiwelengero cha anthu ambiri onwe akupululuka ndi HIV ndi ansembe a Roman Catholic. Ansembe akuononga mabanja m’malawi muno. Kudzudzula kwa mwanoku ndi kosadabwitsa chifukwa the word Msusa is a translation for opposition. Mkulu ameneyu anachita chimodzimodzi Ku Providence Secondary School. Ansembewa amusokoneza Chilima who was the undisputed DPP presidential candidate in 2024. The entire Chilima movement is infested with catholics. Mwamulakwira Chilima. Ansembe musiye kuononga mabanja a eni. Ambuye mulembe chikalata chodzudzula a nsembe a Roman Catholic ndi khalidwe lao la chiwelewele komanso kupha ma alubino. Ambuye Ziyaye chinali chitsanzo… Read more »

Ndidzaulula
Ndidzaulula
5 years ago
Reply to  Hatton

Original Bishop anali a katundu a Chiona si za Chinazi zonamizidwa ndi azigololo a chi na Mulomole ndi anzawo. Enafetu we have been catholics before jumping ship poona kuti kwachuluka ndikupembedza mafano. Munthu useme thabwa wekha kenako uyatse kandulo nkumaigwadira. Pali nzeru apa? Lero ma Bishop atopa ndikubisala pachipande. Amusokoneza Chilima lero ndi uyu angothawira paguwa ngati Yowabu. Inu simudziwa kuti ngakhale Yowabu adakakamira gome koma adagwazidwira pagome pomwepo? Kulephera kuzuzula ansembe awo akufalitsa edzi mmamizimu ndikumangobereka ana a pa tchire. We know you in and out ngati mukufuna kuti tinene zambiri ma bishop nenani. Kenako tidza bweretsa data ya… Read more »

Lookout màsuku
Lookout màsuku
5 years ago

Peter Muthalika is a savage and a thief

DPD A & DPD B
DPD A & DPD B
5 years ago

Chilima and Pitala ndiamodzi. Yina DPP A yina DPP B.

Akhala limodzi all this time. I don’t think a true member of MAP would go to Chilima. Amene akupitawo ndi a DPP okhumudwa. Agawana zida.
Viva MCP

Mesimadzi
Mesimadzi
5 years ago

Asatinamize awa, a few months ago they used foul language against former pope Benedict the 16th and those behind the distribution of a cloth bearing the former pope’s face.
The Malawi Catholic (but the church is actually Roman Catholic) is also on record gagging the ministry of education not to allow Mdalitso wa bodza as part of literature books to be studied in Malawi’s secondary schools. Ngati mukufuna kuimitsa kandidenti wanu pachisankho imitsani, tidzamunyenyanyenja pa May 2019.

Read previous post:
SKC, APM come face to face Monday at Malawi Investment Expo

President Peter Mutharika will come face to face with his deputy  Saulos Chilima who last week open up about his...

Close