Congrats nyamilandu.ndidanena kale kut big apambana.vuto ndilot yabwanya samausata mpira bolanso max.mwini wa max bullets.amijiga amakamba zakale kale zosagwirizana ndi nyengo yomwe tili amangot azitafuna za famu ooomoh mwauponda.amijiga adazipangila okha de campaign nyamilandu adawapasa mwai awonese luso koma palibe adachita olo ku intervyu adapara bwenz ntchito zawo zitawachitila umbon koma ai palibe mMalawi samaziwa kut mu udindo wa nyamilandu mafana adatenga chikho eeeeemuli momuno?
WANYERERE
8 years ago
Nyasa Times please censor your articles before publishing. Which heads are rolling at wanderers? We are remaining with two games to wrap up the season and you come up with this nonsense to demoralise the technical panel? Let them finish the season misecheyo pambuyo. Infact kananji has performed we won the carlsberg cup and reached finals of the std bank .
Jack Muhura
8 years ago
Elia ananena za mwano pochoka ku BB ndiye ndisamve kuti akubwelera. Him is not a player and has never ever played a competative ftbo akagwere. Kochi ndi Ramadhan osati zinazi anaisintha BB nkuyamba kugoletsa mosavuta.
Mphwache
8 years ago
Ma officials a Wanderers were busy kuyangana ndalama.
Yes,I agree with this decision of sending Kananji on a recess for he has failed us.He does not hav the technical know how he is just luck.
Congrats nyamilandu.ndidanena kale kut big apambana.vuto ndilot yabwanya samausata mpira bolanso max.mwini wa max bullets.amijiga amakamba zakale kale zosagwirizana ndi nyengo yomwe tili amangot azitafuna za famu ooomoh mwauponda.amijiga adazipangila okha de campaign nyamilandu adawapasa mwai awonese luso koma palibe adachita olo ku intervyu adapara bwenz ntchito zawo zitawachitila umbon koma ai palibe mMalawi samaziwa kut mu udindo wa nyamilandu mafana adatenga chikho eeeeemuli momuno?
Nyasa Times please censor your articles before publishing. Which heads are rolling at wanderers? We are remaining with two games to wrap up the season and you come up with this nonsense to demoralise the technical panel? Let them finish the season misecheyo pambuyo. Infact kananji has performed we won the carlsberg cup and reached finals of the std bank .
Elia ananena za mwano pochoka ku BB ndiye ndisamve kuti akubwelera. Him is not a player and has never ever played a competative ftbo akagwere. Kochi ndi Ramadhan osati zinazi anaisintha BB nkuyamba kugoletsa mosavuta.
Ma officials a Wanderers were busy kuyangana ndalama.
Ananena kuti akubwera ku Bulllets? Shame on you.
Pa Easy Manoma, we r already in Top5….
kananji ndiye upeze kopita ku bullets kwathu takana