Email a copy of 'Health worker arrested over drug theft, granted bail: Updated' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

6 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nyoni weniweni
8 years ago

a 2 Ellias , wapenga misala ndithu, yemwe ukumunenayo amagwira ku Dream ufufuze kuti amamulipira ndalama zingati and wagwira ntchito zaka zingati ndi salary yakeyo kuti sangagule galimoto. Just try to work hard man ndizotheka.

alhomwe atilaula
alhomwe atilaula
8 years ago

Just imagine muthu zaka 22 nkumaba pantchito chonchi? What more komwe atadzafikire zaka 30? Kenaka aziti boma likulephera kugula mankhwala nzipatala! Its really sad ofunikadi anthu amenewa kumangoachotsa ntchito basi. Abusa chonde tithandizeni mdziko muno muli mzimu wachilendo wakuba pena pali ponse, even christians chonde tiyeni tepemphererane, Malawi is in great need of healing, mzimu umenewu uchoke otherwise dziko lino silizapita patsogolo! Shame on all you people who r busy stealing mankhwala mzipatala! May God punish u severely!

Rift Valley
Rift Valley
8 years ago

Thefts will never stop as long as we target ‘small fish’

Dikisan
Dikisan
8 years ago

ACB nkhani ndi imeneyo yambaniponi. Ngati mufuna umbani wina forum ndiyomweyino. Tikuuzani.

Ellias
Ellias
8 years ago

Alipo ambiri ogwira ntchito mu zipatala omwe akumaba mankhwala nkukagulitsa ku pvt clinics. Wina ndi mwiyeriwa ali ku balaka within a spate of 2 years has managed to buy 2 cars and a house. How much is his salary? Pitani kuseli kwa Mulanje district hospital, you will find big and neautiful houses zomangidwa ndi ogwira ntchito ku chipatala. Monitor pliz no wonder mankhwala akusowa.

B MATSAUTSO
B MATSAUTSO
8 years ago

Mufuna mutimphimbe kumaso tikuziwa mumusiya ameneyo. Woyamba siameneyo wina kuphalombe komweko anaba masolar panel apacipatala ca nazombe anagwidwa nawo koma pano anamusiya amupasa transfer kupita kuciteketsa health centre. IFE TIKUKUWONANITU ZIMENE MUKUPANGAZO. A ACB TAWAONANI BWINO AMENEWA.

Read previous post:
Bucci gets the best on debut mixtape ‘Worth the Wait’

R&B musician Bucci has roped in the cream of Malawi’s urban music in his forthcoming mixtape Worth the Wait. The 20-track...

Close