Email a copy of 'Hiwa exposed again: Roads Authority CEO in more procurement scandal, K80mil from Fargo as govt stops ACB probe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Hiwa exposed again: Roads Authority CEO in more procurement scandal, K80mil from Fargo as govt stops ACB probe' to a friend
Using a normal political calendar, the DPP honeymoon ended on June 1, 2016. That is when it clocked two years...
Ndinanena kale kuti vuto ndikuti a Hiwa munakwatila mkazi okongola ndiye ena amamufuna koma akawakana basitu nkhani yakuti inu mukalowe kundende apeze mpata iwowo.
A Malawi tilibe nazo ntchito izi. Musiyeni aziba munthu. Azigawana ndi omuteteza anone mafuta munthu.
kumanga koma muzimanga onse aku opposition and ena onse odzudzula boma. ACB and MRA kuteroku nkhani ngati izi kukhalira koma kusaka onse otsutsa boma. kenako tikubwererani mu manyumba mwanu tsopano
abala nsanje pamalawi sizatha, who are spreading these stories…..musiyene munthu
Tungosauka opanira mphika ali chete
Cashgate sizatha ku Malawi chifukwa akulu akulu akupezamo cholowa! You can run but you will never hide! The 40th day will come!