Email a copy of 'Husband kills wife secret lover in Mangochi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Husband kills wife secret lover in Mangochi' to a friend
Malawi Electoral Commission (MEC) chairperson Jane Ansah says the pollster can only use the 50+1 electoral system in the 2019...
akanangowugwira mtima mwamunayo.and because we ‘ve different level of temper …
Ndilibe mau!
uyo wafera ntchito zake, koma run away husband anali kale ndi plan yomugwira mkazi wake red handed,,,chifukwa ankadziwa zomwe amapanga mkazi wake, ndiye akazi muchenjere mukamapanga zanuzo,,azibambo masiku ano Ali tcheru ndithu..
Iiiiiiiii !!! The world is just too small for him now, he can run but can’t hide.
Two big mistakes: kudyera mnyumba mwamwini wake, komanso pa bed lamwini wake. Anaonjeza. Anyway, dziko ndi anthu ake.
wafela zaeni, osakhitsidwa ndi zomwe mulinazo……..apeleke phunzilo kwa adyela enawa
Chitsiru zedi iwe wonyenga wamwini mkazi…amatero
It’s not good to take the law into your own hands,the killer has to be charged once caught
deserved it .with all the unmarried ones ,what was so special with the married bitch
The wages of sin is death.
Amen
Kafa katalawa. Akapezana Ku Jahena komweko koma winayu watsogola kukakonza malo