Email a copy of 'I killed my sister, witchdoctor told me to remove her private parts to get rich... suspect tells Malawi Police' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'I killed my sister, witchdoctor told me to remove her private parts to get rich... suspect tells Malawi Police' to a friend
Board Chairperson for Umodzi Holdings Limited, Francis Mbilizi Friday said they have long term goals to develop the Umodzi Park...
Chonde anthu aku Mchinji sinthani nkhalidwe wanu
wakuphayi komanso sing’angayo onse amangidwe chifukwa akulakwisanso kwambili ndi ang’anga achinyengo ngati amenewa
Iwe zangazatha,ukati achewa alibe zelu iwe ulindizelu?Kupanda nzelu kokhakokha.Anthu osakhana mitundu pamene muli AMALAWI.
Judge not, God hidden two things from us and these are the day of a person’s death and a way a person may get rich.
Thanks the police for apprehending the suspect and is good that he is admitting to have done the killing of the innocent sister of his. May justice take its course as God is punishing him for the wrong he has done( Exodus 20:13)
Umbuli shame mw wathu witchdoctor must be arrested n lay charges for muder,a satana oipa inu
Amapanga zimenenezoyo ndi savege, osaphunzira. Munthu opita ku School sangapange zimenezo. Tamuonani nkhopeyo munthu opita ku school angapange zimenezo!!! Coz munthu opita ku school aganiza kaye kawiri katatu!!!!
The witch doctor must be arrested at once. He is the one who led the idiot to kill his sister, and they both must rot in prison.
Kodi achilombo chimachi sichidzamaliza anthu? Shame on you devil
Achewa kupanda nzeru