A Chihana, siufumu uwu woti umayenda from father to son. Anthu ngati sakukufunani vomelani. Pali zambiri zimene mutha kumachita. Mukhoza kuyamba business yowotcha tchipisi kapena kumapha mbewa nkumagulitsa m’mbali mwa misewu. Apo ayi kumasoka mphasa and earn a living.
Kodi a malawi tinakhala bwanji? Even though iyi ndi northern region issue koma the pattern is the same. We never learn. si exactly zinabalalitsa aford yomweyi nthawi ya chakufwa ija? Nnse ma president awirinu mbuzi. Hold convention ya bwino bwino although you will not achieve anything. Next thing one faction will go to dpp the other to mcp chipani kuthera pompo. Exactly mmene chinathera poyamba paja. Please my educated northerners sukulu ndi nzeru mumadzitama nazo zija ndi chonchi?
Banyithu ku Aford kwasuzga these two presidents have given the press a lot of work the press is not sleeping on its job zipani zizatha ngati makatani were the unerring remarks by Bakil today all the political parties formed at the dawn of multiparty system are being haunted by these words yet the founders are still alive this is a terrible prick on their legacy the balloons are being deflated
TRUMP
5 years ago
WHY DO PEOPLE RESIST/BLOCK CHANGE ??
I THINK THESE LEADERS TAKE ADVANTAGE OF THE POOR MALAWIANS
THEY CAN’T DO THIS NONSENSE
IN ZAMBIA
I RESPECT THE PEOPLE OF ZAMBIA # THEY WERE THE FIRST PEOPLE TO TELL MUGABE TO
GO GO GO !!
band yagawana zida. Lets listen to what each leader what somg he will play!!!
Mapwevupwevu yanjira mu AFORD. Tamuphalilaninge kuti munjilenge ma virus mu AFORD. Mwaziwona sono!!!!!
Thats why i have never liked this party. Ine ndili nganganga pambuyo pa Yudiefu. Chipani changa
Koyamba kuona anthu kukangganila Chinthu chakutha
Za atumbuka !
A Chihana, siufumu uwu woti umayenda from father to son. Anthu ngati sakukufunani vomelani. Pali zambiri zimene mutha kumachita. Mukhoza kuyamba business yowotcha tchipisi kapena kumapha mbewa nkumagulitsa m’mbali mwa misewu. Apo ayi kumasoka mphasa and earn a living.
Kapenanso ya kabaza.
Atumbuka mubelane timabriefcase party tanuto.
Kodi a malawi tinakhala bwanji? Even though iyi ndi northern region issue koma the pattern is the same. We never learn. si exactly zinabalalitsa aford yomweyi nthawi ya chakufwa ija? Nnse ma president awirinu mbuzi. Hold convention ya bwino bwino although you will not achieve anything. Next thing one faction will go to dpp the other to mcp chipani kuthera pompo. Exactly mmene chinathera poyamba paja. Please my educated northerners sukulu ndi nzeru mumadzitama nazo zija ndi chonchi?
Banyithu ku Aford kwasuzga these two presidents have given the press a lot of work the press is not sleeping on its job zipani zizatha ngati makatani were the unerring remarks by Bakil today all the political parties formed at the dawn of multiparty system are being haunted by these words yet the founders are still alive this is a terrible prick on their legacy the balloons are being deflated
WHY DO PEOPLE RESIST/BLOCK CHANGE ??
I THINK THESE LEADERS TAKE ADVANTAGE OF THE POOR MALAWIANS
THEY CAN’T DO THIS NONSENSE
IN ZAMBIA
I RESPECT THE PEOPLE OF ZAMBIA # THEY WERE THE FIRST PEOPLE TO TELL MUGABE TO
GO GO GO !!
Is Mugabe from Zambia ?? I know he is former president of ZIMBABWE not ZAMBIA.
CHIPANI cha anthu amisala.