Email a copy of 'IMF gives positive rating to Malawi economic performance: Confirms growth, inflation remains low' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'IMF gives positive rating to Malawi economic performance: Confirms growth, inflation remains low' to a friend
Malawi Police have arrested 15 Ethiopians at Dzaleka refugee camp in Dowa in a violent operation which saw the refugees...
a mw amandisekesa. THEY DRESS TO IMPRESS.
LIP SERVICE AMAIZIWA. AZUNGUO SADZIWA MMENE ZINTHU ZILILI KUNO/
SKOMO
Bravo my country, bravo my government, bravo APM bravo nyasatimes for writing this story without fear or favor. While we are waiting for MCP presidency and its supporters to oppose this because that’s what they are good at, i couldn’t care less, ndi anthu otembeleredwa osafunila dziko lawo zabwino. Ikakhala UTM i wonder ngati amadziwa chilichonse zokuza za chuma, i mean ngati akulephera kudziwa malamulo olembetsera chipani mdziko lawo lomwe.
Galu chilima must read this good news about APM.
The fruits of having a wise leader APM is the man his action speaks more louder than words….no doubt my vote is for you and DPP come 2019.
Aaaaah aaaah! komatu izi ndi zonvetsa chisoni kwambiri. Akukadziwa azungu mpaka kuyamikira kuti economy ikuyenda bwino ndipo chuma chikukwera, pamene ife eni ake tikumangonyoza, osadziwa zoona? Kodi ndi chifukwa cha nsanje, kapena umbuli, kapena ndale? Tiziti a Mtambo ndi a Trapence amadziwa zachuma (economy) kwambiri kuposa a World bank ndi IMF kapena? No no no guys lets change course (track or path) Nsanjeyi will take us nowhere akuluakulu.
IMF is a lending institution just like National Bank. Since Malawi has no credit rating institutions investors or donors depend on them for information. So what they are saying here Malawi akhulupilika kubweza ngongole
Oohhh yeeessssss!
Muwauze neba za izi. This is IMF analyzing our economy and have given a positive report. We have organizations here who only focus on the wrong. Work up and let us pull towards one direction. Achina Mtambo ndi Trapence
Amene mukumanyoza professor tanananitu timwe. DPP 2019 Boma