Email a copy of 'Immigration suspends printing of Malawi Passport' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

49 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Elliot Matiki
Elliot Matiki
9 years ago

There Z no nid 4 u 2 increase pasport cz their ppo they r struggleling

Mark chikweni
Mark chikweni
9 years ago

Kwerani za Mangochi opanda chiphaso mukafika ku Rsa.

chrisstopher shangire
chrisstopher shangire
9 years ago

You charge too much custom when when we are coming back to our buetiful land

son
son
9 years ago

Mfwethu izi sozoona ukapita ku rsa lero ukapeza amalawi ambiri.pali maboma awiri mzimba ndi mangochi.ukafika ukhoza kuva chisoni ena satha kulemba or kuwelenga munthu ngati sanapite ku sch angakagwire ntchito yanji kwaweni.munthu kungo vota lero mawa ali bus,kungokwatila lero mkazi akumusia ndi makolo eye wa ku joni,podzabwela after 5yrs.pepani sindikunyoza abale aku mzimba kapena mangochi koma chilungamo chake ndichimechi.tiyeni tichepetse kubeleka boma silikwanitsa anthu tachuluka ndichifukwa chake tikuthawa mdziko lathu chifukwa chamavuto.

mpamba
mpamba
9 years ago

sorrial

Mfwethu
Mfwethu
9 years ago

There are so many people who got passports but have never even travelled. And then there is this expiry issue, you find other passports expiring with so many unused pages…

son
son
9 years ago

Amalawi tamavetsani chilichose kunyoza,ukapita ku immigration aliyese ukamufusa kuti mukufuna passp mukupita kuti uyu akuti rsa.kodi ndi choncho.akakuwuzaniso kuti rsa sakufuna obwela munyozaso.ndichifukwa chake akukuwuzani kuti kulibe ma passp.ingoganizani bwino

Patriot
Patriot
9 years ago

And ya amwenye is K500,000/person, koma alibe stationary.
Amangodya ndalamazo eti?
ACB ifufuze zoputsazi.
Malawi ilidi mmanja mwa agalu

Mberube
Mberube
9 years ago

Kwangu NO 37 CHANGE IN Management meaning abweretse another homwe? We dont want… Last time that Lhomwe was here all he was doing was enriching himself. Tiulure za GUN-GATE? UNIFORM-GATE? PASSPORT PRINTING-GATE? File ilipo… Mankhwala was just a good person osamumangisa …

James Phiri
James Phiri
9 years ago

Last year Immigration took more than 3 billion Kwacha in revenue but now has no money to print passports. This is mis-managament. Anyone getting fired anytime soon – no didn’t think so. Seems like the president’s passport to travel is unaffected by this lack of passports. By the way Mr President any chance of you declaring your assets anytime soon. We’d like to know what you had before you became President and how much you have 1 year after becoming President. The increase in your assets should be equal to your annual salary plus 1 wife.

Read previous post:
IOC trains 24 Judo coaches in Malawi

Twenty four local Judo coaches at the weekend graduated from a weeklong Judo coaching course at Kamuzu Institute of Sports...

Close