Email a copy of 'Irish President jets in Malawi for state visit' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Fathara
Fathara
9 years ago

Akalandilidwa ndi a president NKHUMBO KACHALI ndi achiwili awo a CHIHANA akapita ku NYIKA. Ife kuno ku Malawi sitikuwapoyilila wachepa ameneyo.

Yobe boo
Yobe boo
9 years ago

KOMA NGATI MU DPP MULI MUNTHU WONYATSA, NDIYE CHAPONDA.

Kanyimbi
Kanyimbi
9 years ago
Reply to  Yobe boo

Koma ukanadziwanso kuti ngati pali munthu wonyasa kwambiri pa dziko la pansi ndi bambo ako sukanalemba izi. Shaaaa! Haram.

Bantu
Bantu
9 years ago

I am DPP, but I like the way APM’s presidency. Well done Mr President for delegating on these trivial matters and for restoring dignity in Malawi’s first office. All around the world, presidents don’t waste time welcoming guests at airports.

Angozo
9 years ago

I personally do not see any problem for Chaponda to welcome the Irish President. It is normal, only those who always born to oppose anything can see a problem kodi a malawi enanu munakhala bwanji za zii.

Chikopa
Chikopa
9 years ago

AMumafunsa kuti why sanapite kumaliro apa mukutukwanabe kodi amalawi tizikhala choncho wina akuti musapeleke chithandizo koma iyenso iliku malawi anthu akuda munakhala bwaji mukupitiliza zomwe mumapanga 2010 ndimayi wanu jb malawi is geting poor and poor inuyo chimene mumapindula ndichani. Tizichedwa ndikukangana mapeto ake tisowa chogawana please masakho apita maso athu pasogolo, azungu kuti atukuke amapanga chimodzi teyeni tisegule maso tisamagonebe

chilungamo
9 years ago

Matako ur comment is Satanic, u r one of those people who would stop the government from funding Prisons becoz taxpayers should not feed criminals! Ife tikuvutika koopysa ndiye iwe ukuti Irish Government isatipatse chithandizo, chamba chani? That’s really backward! Most of the times when our President goes for a State visit especially to developed States he is not welcomed by the President/Prime Minister of that country! Its usually the Minister of Foreign Affairs or State! There is nothing unusual here but u guys kusonyeza umbuli

Fathara
Fathara
9 years ago

Ife a boma la DPP sitikunyengelelanso nzungu wina aliyese tilibe nawo ntchito akagwele uko. Apa zikuchita kuwoneka kuti boma silinamuyitane, wabwela kufuna kwake. Akatelo azitiwuza kuti tizikwatana amuna okhaokha, akazi okhaokha basi, ali mukapanda kutelo sitikuthandizani. Mumatiyesa ife zisilu zanu eti? PETER AZAKAMUCHINGAMILA PRESIDENT PUTIN NDI WAKU CHINA, OSATI ASATANAWA. KODI MUMATI KAKAMILA BWANJI MUMAFUNA CHANI? IFETU MULUNGU ATITHANDIZA ZITHU ZIKHALA BWINO MUZACHITA MANYAZI YEMBEKEZANI.

Ingwina Sya Karonga SC
Ingwina Sya Karonga SC
9 years ago

He has just cancelled the trip to Zambia, expecting the Visitor.
Now he is even delegating to the Airport, then later he will also send somebody to State Banquet.

Ingwina Sya Karonga SC
Ingwina Sya Karonga SC
9 years ago

Delegated the HE is reducing costs kkkkkkkkkkkkkkkkkk

Tsamba Likagwa
Tsamba Likagwa
9 years ago

Zinthuzitu kumazitsata. President salandila President zake paairport. It is the duty of the Minister in waiting to do that unless he himself decides to do so himself. Otherwise it is not a must. The minister in waiting presents the visiting President to the Welcoming President at his official residence. Even akamapita ku Salima ko plus malo ena otero azipita the Minister is waiting not the President. Monga ndikunama. Sizinali choncho even nthawi ya Madala Angwazi? Mabulutu inu including no 11 osamaonetsela ubulutu wanu pa net pano. Kumazitsata izi

Read previous post:
Kamuzu Central Hospital suspends operations over water crisis

Kamuzu Central Hospital has suspended all theatre operations and others clinical works that require running water because of water crisis...

Close