Email a copy of 'It’s Mighty Be Forward Wanderers, K70m deal for Malawi football giants' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'It’s Mighty Be Forward Wanderers, K70m deal for Malawi football giants' to a friend
Premier mobile phone company TNM has donated K1 million to Malawi Law Society (MLS) as contribution towards a symposium on...
timatimu ta kwathu ka club house ngati garage
Mine is just congrats To Be Forward for your rescue and my appeal to Wandereres management to use the finance suport properly.Lastly,its a request to the govt.WE need stadium in South pliz.
Nayo bullets yapeza sponsor wawo it wl be cald ‘rangers security bullets’logo yawo ndimutu wagalu
Proud of u manoma!!!!!!!!!!!!!
Manoma thandizo mwaalandila koma muchepese kusolola
manoma ndi deal
Tsopano ndipofunikira kuganizira aneba, ngakhale Boma lithe kulowelerapo, tangoganizirani ,ku Lilongwe : Silver,Civo ,Blue Eagles ,Kamuzu Barracks, Mafco ,Ma team othandizidwa ndi Boma okhaokha,komanso ma Studium atatu sopano Silver , Civo ndi likumangidwa kumene lija, pamena ku BTz kulibe team yothandizidwa ndi Boma kupatula mikango yaku Eastern Region, Kunena za Stadium ndi ija Mayi wamatewe uja, ndinena mbava yayikuluyi,ndinena Mayi uja analuza ali m’bomayu , unu ujayu, analandisa Stadium kuno ku mwerayu kutisiya pa mbalambanda opanda Stadium ati koma nkumafuna kuti tivotere ife aku mwera. Zausiru
usova wekha ndi kumwera kwakoko. kwa ife pa kapitolo,inde, LL, mayi ukunenayu ndi nyatwa. capital ikukongolerakongolera ndi chi stadium nyatwa, nyanga chikati chatha, u wil never taste an international match in the south,pepani.
Mphwanga DPP ndi deal, imanga Stadium kawawa kuno ku Malawi, kaya zako izo ndi Matiki Chakwera wakoyo , m’busa wa feki
Am a BB fan, but lets congratulate our friends for making it. Its not easy as we all conpeted for it. Lets pray for rest to hav also sponsorship.
Apa ndie manoma aiphulatu. congrats!!!!!!!!!
Sound gud 4 me