Email a copy of 'Jane Ansah not resigning: Malawi Electoral Commission accuses CSOs of ‘distorting facts’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Jane Ansah not resigning: Malawi Electoral Commission accuses CSOs of ‘distorting facts’' to a friend
The National Switch Limited (Nat-Switch) has bemoaned failure by some member banks in adhering to rules and standards set by the...
Biased CSOS, nthawi ya Amai anathawa aja, where was Sembereka, Trapence, kungoti onsewa except Mayaya. Vuto la Mayaya amasatira a mfumu kuledzera.
These CSOS, including Dorothy Ngoma are crying for the cashgate money they were eating with Amai anathawa aja.
If you don’t know, Amai aja lost the election chifukwa amagulitsa dzikoli kwa atumbuka
DPP and MEC don’t care whether laws are broken provided their interests are saved.They are ready to face the cosquences.Kaya ndi zibonga kaya ndi zikwanje, they are ready.This is thw time to test waters.Come 2019, mudzaonanso. Chisankho cha 2019 sichichitika boma libe ndalama.Choncho bomali lipitila kufikira pamene zidzapezekere.Imeyo ndiye DPP. It has injested UDF which is digested,the absorved followed assimilation and then excreted as the waste for sake of silencing MANGOCHI,no nosence district
Ntumbuka =CSO
Mlomwe = Boma
Nchewa = Opposition
Nsena+Nchawa= Chubwi m’madzi
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
dziko ili tigawane basi
Billy Mayaya, Gift Trapence, Dorothy Ngoma, Robert Mkwezalamba, Rev Macdonald Sembereka, Leon Matanda and Desmond Mhango –
a YAKI…. kodi apa a Tumbuka ndi angati ? kodi mukati aTumbuka ….what do you mean ?
MALAWI DZIKO LA MATSIYE (A LOMWE ESTATE )
KUMVESA CHISONI !
NOTHING IS MOVING
FORWARD RATHER BACKWARDS !!
Pamenepo ndiye pa Malawipo. What facts have been distorted here? The Electoral Commission can not run by-elections becoz the Gavamenti has no money. To hell with democracy. And the Electoral Commission would Malawians to buy this. Someone does not want the by-elections to be held. The Chairperson is dancing to the tune of that someone.
Kma ma comment Ena amangoonetseratu how some behave even if you have not met them ..malawi nation and its people…
Kodi ma CSO onsewa, ambiri ndi a Tumbuka okha okha bwanji? Nanga A Lhomwe akudzadzana bwanji mmaudindo okha M’bomamu? Kaya ine Mchawa Nsena chubwi ndamira.
In chewa there is a saying which goes like this ” Chitsiru chili ndi mwini “. No wonder this mec official is backing Jane Ansah’s incompetencies.