Email a copy of 'JB Foundation donates relief items to Malawi flood victims' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'JB Foundation donates relief items to Malawi flood victims' to a friend
Chairperson of the Episcopal Conference of Malawi (ECM) His Grace Bishop Joseph Mukasa Zuza has died in a car accident....
Mayi wazero inu pakana ifa tili nanu athandizeni azathuwo ife kuno ku nkhatabay mulungu watikondela koma azathu akuvutika athandizeni
Amayi tikuyamika pitilizani ntchito yanu ya umayi.Dziko lino likufunika mtsogoleri monga Joyce Banda.
This is just giving back to Malawi what is Malawi’s. It is part of the K20b cash-gate, K75m nac-gate and a little from jet-gate. No need to blow own trumpet.
That’s JB always caring we really appreciate dear mama whether Malawi or us ur always there to help keep up the good work
Bweza za cash gate .
A Bwinchombe kupepela, wakuuzani ndani kuti JB wathawa? Aleka kuthawa mbwiyanu kamanoyo
chitsanzo chabwino chimenechi
Keep BLESSED
Eya eya eya koma pamenepo. Ine mai uyu amandiwaza zedi. Zathu za cashgate zayamba kubwezedwa. Nonse okhuzidwa ndi cashgate mutengele chitsanzo chabwino cha mai.
Zaziii. Tsopano wathawamo chani m’dziko lake lomwe?