Email a copy of 'JB hits at DPP govt for failure to finish projects' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'JB hits at DPP govt for failure to finish projects' to a friend
Girls Empowerment Network (GENET) has assisted over 100 girls with bicycles in Dowa District since 2017, to ease their mobility...
Tawawudzeni zowona a Mayi, a DPP ndi Pitala anawanamiza anthu aku Nsanje kuti inu munakhalira Nsanje Port ya malemu Bingu, koma Pitala chilowele mu boma pano 5 years alindwiiiiiii pankhani ya potiyo.Komanso nkhani ya Cashgate a Goodah nthawi yija mu 2013 akayasamula nayo kukamwa mpaka kuwonesa mano ose koma pano ndimwana yemwe MuMalawi muno akudziwa kuti ngati pali boma lakuba kwambiri ndendi DPP, macompensation osadziwikabwino kwa Mulli, anatigulisila MSB Bank kwa Mpinginganjira, mapayment achinyengo ku Police ………
But Amama JB you failed to take on NB hospital and Mzuzu -NB road projects which Bingu had left at infancy stage. Do you know that your inactivity on these projects cost you dearly?
Abiti Ntila nzeru njeeeee. Two years why didn’t you end the quota system?
Congratulations DPP for refusing to continue with the cashgate project which JB started in 2012.
What do you mean by ‘ elected back’ You JB have never been elected into government in your life.
Munalowa m’boma kudzera Ku mzengezi.
Amai Chilimatu anakamuona Winiko Ku ndende. Inu mukamuona Lutepo liti Ku ndende?
Inu nanu ma awa anayambika ndi malemu Bingu osati mayi uyu. Iyeyo ndiye analephela kupitiliza ma project
Just ignore this baffoon. He can’t even figure out in his baboon-like thinking head that 2011 came before 2012. On record we have court verdicts of K201 million CASHGATE convicts in 2011 and not 2012 when JB accidentally became president.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkk !!!