Kodi mukamaloza munthu ndi dzanja lanu, ndizala zingati mumamuloza nazo? Nanga ndi zala zingati ziloza inu? God is watching. Freedom is coming tomorrow.
Sos
6 years ago
In this forum grammar does not count. What matters is content. You have already understood the other person wanted to say. Stolen or stolen, Chaponda ndi wakuba basi
Mjcentral
6 years ago
Political Persecution? Osamapanga zoyesa dala.
2019 voter
6 years ago
Those who believe, let us pray that God intervenes in anyway as long as Malawians get their freedom. Amen.
pathfinder
6 years ago
kkkkkkkkkkkjk munyera agalu inu mukudana ndi alhomwe. these are two different issues, unless you know something that maybe chaponda had something to do with a fake resignation letter then yes ngwengwengwe for his arrest. Chaponda paid for his stupid actions, as we both know that he is no longer a minister. Nawenso abit pakunya pako. ukungoona ngati mulungu ndichoopsezela anthu.
Kuchititsa manyazi boma la DPP. Konsekutu kusonyeza kusowa mtendere ndi kusabwera kwa JB. Amai amakuopani muzikhala ndi confidence
Kodi mukamaloza munthu ndi dzanja lanu, ndizala zingati mumamuloza nazo? Nanga ndi zala zingati ziloza inu? God is watching. Freedom is coming tomorrow.
In this forum grammar does not count. What matters is content. You have already understood the other person wanted to say. Stolen or stolen, Chaponda ndi wakuba basi
Political Persecution? Osamapanga zoyesa dala.
Those who believe, let us pray that God intervenes in anyway as long as Malawians get their freedom. Amen.
kkkkkkkkkkkjk munyera agalu inu mukudana ndi alhomwe. these are two different issues, unless you know something that maybe chaponda had something to do with a fake resignation letter then yes ngwengwengwe for his arrest. Chaponda paid for his stupid actions, as we both know that he is no longer a minister. Nawenso abit pakunya pako. ukungoona ngati mulungu ndichoopsezela anthu.
Inu a DPP ndikukumbuseni pang’ono mwina mukuiwala dala kuti Mulungu si Pitara kapena Chaponda! Mulungu akulangeni koopsaa!!
Chaponda Must Face Arrest!!
Malawi is full of idiots!
Kodi mzingomanga otsusa okhaokha days stupid.pitala samala ndi police yako akupweteketsa