Jealous man beats wife to death over ‘cheating’ suspicion
Malawi Police in Phalombe district on Friday arrested a 48 year-old man for allegedly beating his wife to death.
According to police, the man, identified as Ganizani Salondwa beat his wife Esther Salimu 26, to death with a wooden brick mould (Chikombole) on suspicion that she was cheating on him.
Pholombe police publicist, Augustus Nkhwazi told Nyasa Times they managed to apprehend Salondwa with help of the community members.
”On Thursday the suspect went out for a drink and upon returning home at around 16 hours, he did not find his wife as she had gone to her mother’s house within the village,” explained Nkhwazi.
He added: ”This did not please the suspect as he jealously suspected his wife was having an affair with another man.”
When the wife returned home, she found her husband furious, and he started beating her with a wooden brick mould.
People tried to intervene but were threatened by the suspect. They later managed to overpower him.
”She was unconscious at the time they rushed her to Kalinde Health Centre, and was however pronounced dead upon arrival.”
Salimu is said to have died due to severe head injuries.
Salondwa is expected to appear in court soon to answer charges of murder under Section 209 of the Penal Code.
Salondwa hails from Thunga village T/A Kaduya in Phalombe.
Follow and Subscribe Nyasa TV :
Mkazi 26, mwamuna 48? Nkona amapanga nsanje ya kaduka
Chikondicho kuphanaso?kungosiya bwa!
achulukilenje Akazi ku musiya bwanji ngati ndi wanjomba kuposa kukakhala kundende
Viwakazi vili mbwembwe matsiku ano vikusowa amuna ndipo chitsiru china chikulolela kukhala kundende.Tilife ife timangoti mayi mwatipepitsa kenako ndikukanyamula mzozodo wa mbina yake ndikuwukhazika pakhomo.Paja azathu achilomwe kuphana nkosayamba.
Zopusa
Chanalume changati icho ndicho tikuti chinthu chawaka.
Mwamuna Opusa!!!!!!!!!!!!!!!
Chiwanda Ndi chimene chavuta chamulakwisa munthu thats very bad for u Bro wishing u o the best ku ndendeko
Alomwe woye
Comment reserve
this is sad
Tisamakhale choncho,chimenecho sichamuna.Amakamwa mowawo ndicholinga ndizimene wachitazi.Tisamatero!
koma dziko lapitadi why not divorce her but killing is harsh treatment ever
Why doing this? Divorce to such a wife is the way out than
being imprisoned.
Thanks to this news paper to let us know to what people do to their loves one! R.I.P mama ur kids will mis u.
Kusiyana zaka zakubadwa sinkhani ayi. Nkhani ndi yakuti pa banjapo panasoweka chikondi. Bible limanena kuti Chikondi chilibe”NSANJE” Chikondi chimapilira, Chikondi sichizikweza ndipo Chikondi sichitopa.
Bt m is same lyk judge akanangopilila chifukwa kazi wafayo mwina ndiamene akanabeleka kadzi wanga ndilakwala
Khalidwe la alomwe ndi limeneli lompha azikazi awo. Chimtundu chonukha chimenechi .Shatapu!
Malawi,??????. loading…….
Opusa kwambiri mamuna ameneyo . Akaidi anzake akachite naye ndithu
Comment: koma mtundu umenewu eish….
R i p
Boma lindilore ndikamuphe ndichikwanje chifukwa wandikwiyisa kwambiri, komanso lamulo loti wokupha aphedwe likanabwelera.
zodandaulitsa ndithu.
No this is very bad. Bible limanena kuti ngati mkazi mwamugwira ndi chigololo musiyeni osati kupha ayi. Apatu Bwana mwawayamba mavuto komanso muli ndi mwazi mmanja chabwino mnchiti apa??
Akaziso muziona pokwatiwa, nanga mpakana 48 against 26?
Vuto lomakwatira atsikana achichepere ndi limeneri. Zaka zanyanya kusiyana nanga wina 48 wina 26. Mkaziyo anali akadali ndi moto pomwe madalawo mphamvu zayamba kuchepa. Ndiye akuganiza kuti poti iwo zikuwavuta basi mtsikanayo akukayang’ana achinyamata a size yache othamanga magazi pomwe mwinanso si choncho iyayi.
Panalibe petrol kuti muchiwotche
Mkazi anali ndi zaka 26. Amuna ake 48. Zikuonetselatu kuti amunawa adakwata mwana ndiye ku Bed so zimawavuta. Judgement I H L.
where is Malawi going everyday fucken stories eish mwanyanya opus nzake kill him other people can take phuziro pang’ono
beer yonse balala, uziona man!!!
he is favourable enough to be jailed for life….very sad to the deceased.
he is favourable enough to be jailed for life….very sad to the diceased may he soul rest in peace.
Age difference was a problem in this case.
i blame the why waiting untill things went out of hand here now life lost. RIP salimu but the man should also face death sentence.
Please government should bring death sentence so that anthu opha anzawowa nawonso azikaphedwa. Osangomusiya bwanji mesa anakumana okulakula, ameneyo akufunika aphedwe ndi miyala pomugenda in public. Ufiti chani?
Why This Hapenning At My Home District Plz? Ndachita Manyazi
worse still the deceased was pregnant.very sorry
mphoto ya uchimo ndi imfa/
mphoto ya uhule ndi imfa.walandila mphoto yake mkaziyo man inuyo mukakhala moyo wanu onse ku ndende kuma moyo mulinawo.
Alcoholics! no confidence iyeyo ndamene amnynga and he turns it round onto the lonesome woman who has to find company from her mother!
Mowawo wagetsa ndiye poti zukukani mwayamba kulota kuti anzanu akukubelani! Its a case of you sire failing to conduct your own marriage succesfully and you kill your poor wife instaed of getting help!
I hope you rot in jail for the rest of your life! She did not deserve to die even if she was cheating you! Milandu amkamba!
Savage to the core! I hope you have a long sentence in jail!
Koma bambo ameneyi anaonjeza , zaka zosiyana mpaka 22 . Mkaziyunso kodi anafela ndalama pomulola mwamuna ameneyi ? Mavuto azonsezi ndi amenewa . Mkaziyu ndi mwana so bamboyi maganizo ake ndiongoti akuyendanso with anothe man coz ndi katsikana .
Bambo woipa iwe . Mpaka kumupha mzako ?
He has to face the music no matter what.
Very bad and un called for ,he deserve to face death too .
that was babaric and the offender must be convicted to death also.
Very bad decission. It would have been avoided. However that is typical work of the Devil. Kwake ndi kupha, kuba ndi kuononga. May her soul rest in peace.
Is this love? This man deserves great punishment
The age gap was huge hence the jealous. Azibambo muzitenga ua agements kuti nsanje ichepe.
Ineso kwathu ndikuphalombe konko, koma sitingachite zopusazo nsanje, nsanje yachani ndiye mpakana kupha ha!ha!ha!ha!ha! ameneyo apasidwe 20 years in jailed, zoba ameneyo eti!
Mwamuna weniweni samenya mkazi. Ngati zinthu zavuta ndibwino kusiyana mwamtendere kuti aliyense akapezenso nzake wina wokoma!
Chifukwa chake pakufunika makako kuti anthu amenewa azinyogedwa
Useless man. Bwanji nawenso osangobweretsa mkazi wina umuswire. This is what happens when men stick to one woman. They become obsessively jealous and end up doing stupid things. Monogamy is not natural for a man.
Codi okhuta mowanso amapanga nsanje? Police mo fyre.
Unalekelanji iweyo kupeza lako hule unlike eliminating somebody’s life
Izi ndi nkhanza osati nsanje!
Mbola
Of all men she chose mwamuna almost twice her age!!Nawe chitsiru cha mwamuna kumenya mpaka kupha mkazi zoona.Galuu.
sanachite bwino
Must be punished fully
Sheet men anapangiranji zimenezi
Comment. choipa chitsata mwini
This man has inferiority complex. He does not believe in himself. He has killed the woman leaving children suffering. So sad indeed!! May the soul of the deceased rest in eternal peace.
Mkulu wa ku Candlex akuchitanso zimenezi zonyengana ndi tiana kenaka akadzakula tizizamuthawa. Mapeto ake azatipha. Tiyeni ti tenge a size yathu, chonde achalume ndupita nanu
Ofunika ameneyo alandile chilango chen chen.
Comment: why cant he just divorse her, eeeeesh! Very bad.
He promised her that death will seperate them thats why.
Zilope alhomwe! Zomapha anthu ku ndale zakhazikika pakati pa mtundu wanu. Olo kutakhala ku polytechnic, mumakafikako nkukaphako mwana wa a Chasowa. Kupha simukuwonanso ngati kanthu. Pali kupha, inu simutopa! Mukangofuna kupha, pangavute maka mpaka mumakwanitsa! Azimu akufulatilani…….mungadye maka, simuzakhuta!!!!!!!!!
Shame
Alhomwe nkhanza bwanji?
There is no strength that is comparable to the one that has in holding oneself when in anger.
LET THE SAME HAPPEN TO HIM.
SAD NES + RIP +
Nde Alhomwe amenewo…..nanga mzodabwitsa izi ku ntundu wawo
Alomwe mkhalidwe wawo ngotelo.
shame
Afera kumene anachokera
Chindere chakufikapo
Ahlomwe tsopano! Zochita zawo ndendende atumbuka!
Killing cos of jealous? unimaginable.
Aphedwe basi bambo ameneyi.mwinaso amagona ndi kabudula so mkazi akanatani
Comment Life imprisonment
Pathetic Indeed!
Waphedwayo tinva wina akuti nyonyonyonyonyo! Koma amuna pakati akhala akuphedwa ndikuchitilidwa nkhanza zosiyanasiyana koma kuli ziiiii. Nanji ndiakwawo! Tiona. Koma abambo sikuti ndikuwabakila chifukwa ndi mbuzi ya munthu,satana
Mkaziyo amakwatira ndi size ya bambo ake mkona amupha, 48yrs akakwatire wa 26yrs? A size yake amasowa?
Mkaziyo amakwatira ndi size ya bambo ake mkona amupha, 48yrs akakwatire wa 263ys? A size yake amasowa?
Zikumakhala nkhani when a man does it a woman. Heard of a man killed by wife in dowa cut him into pieces throw them in pit latrine, no story. A woman cuts hubby penis no story. Mbuz ikagunda galu zikusewera galu akaluma iphani nchiwewe . Kaliati uti chani amabingwe
tisamachite choncho, kumeneko ndi kulakwa kungokhala ngati mkaziyo anachita kugula! komanso akayankhe mulandu wina wa defilement chifukwa mdalayu ndiwamkulu kwambiri imagine 48 years versus 26 years. kodi iyeyo a size yake panalibe amakwatira mwana cholinga amudulire tsogolo basi. akalowe basi!!!!!
nayexo aphedwe basi
Nchiyani Kodi Amalawi?
Alhomwe mophiya !!!!!!!!
Started beating her about the head ???
kamba anga mwala. ufiti upose apa abale.
Kaliati, Yatera pa Uta penipeni, naoni abale akowa.
Chitsiru chamamuna and she was not of ur age. May her soul rest in peace
Mwamuna nzathu,what was that?Beating wife to death?It is not you but influence of the devil through drinking.Repent this and be a christian and God is ready to forgive your sin.
Kuononga katsikana 26 yrs vs 48 yrs sorry rip young lady
BEAR is the parent of all vices.when a person is drunk there is a potential tht he can commit of forms of vices.
Opha mnzake nayeso aphedwe basi
Shame on him, may her soul RIP
Komandiye2 kmenya bebs ngati wakuba,,,m’makwatiriranj mxiew!
Life jail no mercy
Azimai osamachoka panyumba bambo akachoka amafuna akupezeni. But the man anadzitengera pena mpaka kupha? mwaonatu tikamati mowa ndikholo lamachimo onse, inu mkumati iyai bola asaledzere ndani amamwa namayembekezera kuti asaledzere? double standards!!!!
Kusaupeza mtima
Alomwe! Alomweeeee!
Vinyo achita chiphwete chakumwa chaukali chisokosa osochera nazo izi alibe nzeru
Alomwe amenewa kukhala kwawo ndiye kumeneku
May her soul rest in peace
We r in the last days. May ha soul rest in Peace.
Age wise is not okey 22 yrs difference. Wayenera kudzikaikira yekha mamunayo but he has over- reacted. May her soul rest in peace
chitsiru unaonjeza 48 ku 26 kapena anali hule?sumamukwanitsatu.
Work of the devil
whole life in prison. no women. depending on masterbation
nkhaza kwa amayi,iye anali kumowa km akumuganizira mzake kt anali kuchigololo mpaka kumupha pamene umboni palibe.Lamulo ligwire ntchito anthu atengepo phunziro
Ntchito za alopwana alomwe. They don’t even value somebody’s life.
age difference is one of communication barriers,azibambo tisamakwatire ana coz we cant understand them,at the age of 26 she still has the afinity to be close with her mum ,now the old man was thinking to the contrary.amabungwe a Mtambo ndi anzanu nkhani nayi isakhale Human right yoyambitsa ma strke,do or say something.very sad may her soul RIP,
Shame
True that, becouse, beating wives, has become order of the day. We actually have, to take care of them, becouse, they look after us.
Komanso azimayiwa akumapanga mwano heavy. Nawoso achepetse ukula mtima