Email a copy of 'Jesus stars at Nomads 4-0 humiliation in DR Congo: CAF Champions League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Jesus stars at Nomads 4-0 humiliation in DR Congo: CAF Champions League' to a friend
President Peter Mutharika has settled to pick Education Minister Bright Msaka as his running mate in the 2019 elections, Nyasa...
Wanderers wammakwalala imautha koma CAF mwachepa muli kutali kwambiri
Neba! neba! neba! walira chokweza, komabe all in all mwina kuno ku mudzi udzalimba udzationetsa ma miracle goals Eeeeeish koma yaaa, AS Vita ndi akatundu omanga ndi mawaya guys mmmmm ine chonene ndilibe mpaka 4 goals kwa tetete?Where were you Malata,Sanudi,Nyirenda Hurry?KKKKKKKKKKKK!!!!!!!
I questioned the reasoning of joining CAF as I doubted the strength of the team. Wanderers failed to beat any of the top four teams last season in all competitions – CIVO, Bullets and Silver. They won the league by beating middle and bottom placed teams.
Koma ndiye kunali kuthamangitsidwa! eeeeeeeeeeeee Manyozo amvekere ziiii zibayo zokha zokha.
KKKKKKKK Tinkanena ife Nomads have no teeth. What an embarrassment?
Neba watichititsa manyazi ku dziko laeni. Unangopita kukavina kwasakwasa!!
Pepani neighbour ! ANTHU aku DRC alibe chisoni ndikubereka kwa anzawo. Kutizimula ana anzawo mosayangana nkhope. Pepani pepani malilo nkulilarana !!!
Sad news for Nomads family. Train hard and become fit for men’s football. Best luck for your return leg match.
Pitaninso mukawachangamirenso monga muja mudachitira muja powaperekeza. Izi ndi zaziii kuno ku Malawi tinacholowera mpira osewera pakamwa osati pa ground ai. Mpaka 4-0 a Madeira munali kuti ndi mzungu wanu uja Osman. Tinanena ife nkofunika kusintha Coach lero mwazioona kuno adzakuthirani 3-0 believe you me.