Email a copy of 'Joyce Banda and Lutepo CCTV footage, Malawi govt surrenders to ACB' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda and Lutepo CCTV footage, Malawi govt surrenders to ACB' to a friend
About six hundred government sponsored students at Mzuzu University (Mzuni) have been sent on an indefinite suspension following mayhem they...
Vuto lake malawi dziko labata ndichifukwa chake kusauka sikuzatha
Zitaze pano nzatonse akwizingidwe jb yo basi
achezera zomwezo mmalo mopanga zopindulira mtundu wa amalawi hhhh 2019 ndipompano achedwa ndi za ma cctv iwo zawo tizazione ndife moto umadutsa komwe kwatsala ntchire
zaka 5 ndiposachedwapa achezera kufufuza za JB moti azipanga zopindulira amalawi bzy doing useless things they are all thieves palibe wabwino
This is rabish
koma chimwemwe ndi wokongola. nchifukwa chake ambiri amamuvititsa ndipo akawakana basi kumusemela zinyau. kwa nonse amene anakukanani tsekani pakamwa apo bii tikuulani. kunyengetsa manyengetsa kwa inuyo, muli ndi umboni? leave her alone to enjoy her life. ndi mayo wamvano waulemu wake.
The truth only the truth shall set you guys (those in government) free. If indeed it is true that you have JB’s and Lutepo’s cctv footages, why wasting your precious time blowing the trumpet. The ealier you act the better the position you are putting yourselves in. Do not politicize everything thinking that you can win people’s minds. That is cheap politics. If indeed you have clear evidence of what you are claiming, bring it to the court of law thus where a person is proven guilty and not on the media. And thus what we are waiting for so… Read more »
Anthuwa asakhale ngati akuthandiza pomwe akutimanga nsalu mmaso onsewa ndi mbava amalimbira mmipando kuti aziba.koma kwa amalawi azanga kwathu kungokhala kusaukaku basi
senseless ,meaningless, useless and stupid people in a wel created land of peace called malawi. mpaka liti limene tizakhale mu uchitsilu?
Take note that the DPP government is doing its best to cashgatedown all the matter .only some of you do not understand what policies this goverment is doing .some of you are just embiciles as far as what good this government is doing .Look ,the goverment is run on zero budget ,we are without international donor assistance but things are running .i should appeal to those striking to take this with real accord .we know that you have been sent by prostitute Kabwira ,a senseles Mhone ,a stupid Ngwira .MUNYA MUONA AKAMABWERA JOICEYO WA KU MAULA BASI