Email a copy of 'Joyce Banda attacks ‘deeply corrupt’ DPP govt: ‘I’m coming back to Malawi, come what may’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda attacks ‘deeply corrupt’ DPP govt: ‘I’m coming back to Malawi, come what may’' to a friend
President Peter Mutharika has appointed board members of the troubled Electricity Supply Corporation of Malawi (Escom) with economist Perks Ligoya...
bwera tikukufuna kuno wakuba iwe. usayese tizakumvera chisoni. unaba zochuluka sitizakusiya iwe ndi roy chule wakoyo.amati kachale kwanu konko.
kodi nanga nkhani ku CIKANGAWA yogulitsa mitengo/matabwa ku ZAMBIA NDI MMWENYE uja .anthu ambili anacotsedwa ncito opanda malipilo utalanda company from that fella mtse……lo uja??????????????????? ana aathu azimai kulephera sukulu. amai abambo kulephera kusamala mabanja ao coz of your greed. imeneyi unangoipsatila kaamba atidye nao anangoikhalila yet umati kukamba zolemba anthu nchito. mwana wako ndi iwe munazuza anthu, mwaocha eskom kuti zacamba unacita zijaso. kazibwera tili ndi umboni ose bwera uone.abale tigwilane manja apa. kodi aliyese angoti poti ndinali ku abroad nde ndikhale plesident! ZACAMBA. BWERA UONE UESA A MALAWI ALI MOMMUJA HULE IWE, SITEPE NGATI N’GONA
palibe chosintha oloko mutabwera abiti hamala,inuo ndi a pitala ndiye bola tizuzike ndi pitala yemweyu.
Iwe Abiti Ntila..nawenso wachonatu chifukwa cha cashgate. Kuba aMalawi anzanga. Yako ija yotakata…kkkkkkk
kodi azatani bakha uyu. ubwere ndi
-ndege yathu
-maina aamene anaombera mphwiyo paja ukawaziwa anyamata okamwera mowa ku Joni. ulendo ku ma Pub a Joni ndalama lolololo
-ndondomeko yomwe ukufuna azapange kuno koz u r just making noise. zumbwe
-kodi ana a MAKANYA unangonama cithandizo, sukuwathandiza coz of your greed. pakamwa ndi pa bomatu
> utazatofotkoza misonkho yathu komwe imapita
Matchona tatopa nawo
DR Moses Ku Central medical stores alipo mafia and giving contracts pa Buy Malawi Campaign to Malawi pharmacies opanda ODPP tendering, katundu is overbought and rotting in warehouses at Central medical stores,. Investigate Dr Moses ACB
Is Abiti Ntila on a self imposed exile or cashgate induced one? Kubha mayi uyu. Ufele konko wamva? Nthawi yako yotakata pa misonko yathu inapita. Go to hell and roast you mother and baroness of corruption.
Ndalama zakuthelani mukufuna muzabe zina pano mgodi ulimanja mwa anzanu kwanu kunatha mai
I have come to the conclusion that Dausi has only three or four verbs