Email a copy of 'Joyce Banda for national development policy: Urges chiefs to be impartial' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Joyce Banda for national development policy: Urges chiefs to be impartial' to a friend
Peace has descended in South Africa following meeting between South Africa National Civic Organisation (Sanco) and Shepherd Bushiri-led Enlightened Christian...
Kodi akuti chaninso Abiti cashgate? Amayiwansotu alibe manyazi eti, siiwowa adachita devalue kwacha atalowa mu Boma? Adabanso ndalama zakhanikhani nkukadyera ku America kuwasiya anzawo (ngati a Lutepo) ali my ndende. Mukufuna mudzabenso zina? Zatha zina munaba zija? That’s the foolishness of African leaders, munatenga ndalama za anthu osauka nkukalemeretsa anthu olemera kale ku New York, Los Angeles, Las vegas, Detroit, Philadephia, Dallas, San Jose, San Francisco ndi ku Washington. Mukanakhala anzeruko mukanadyera mommuno mwanva kuti mwina Malawi ikanapindula inform of buildings and employment. Mbuzi iwe.
Chitsiru chenicheni cha lady cashgater. Busy kugula mango mmiseu ku Zomba anthu akuchinena kuti chingotaya nthawi yake.
NOBODY WAS BORN A POLITICIAN—NOBODY SHOULD DIE A POLITICIAN ANYWAY !