Email a copy of 'Judge Muhara recuses himself from Mphwiyo ‘cashgate’ case' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

23 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MAbomba
MAbomba
9 years ago

Mulanduwu wamukulira Muhara. Nanga poti iye ali ndi mulandu wake wa MRA wa taxborrowgate. Kasambara nso akanadzipanga recuse from representing cashgaters.

Lloyd, nanga new born baby ali bwanji ku Blantyre? Tidakaberekabe?

Abiti Mtila
Abiti Mtila
9 years ago

Mphwiyo does not require bail! once he goes for medical check-up he will not return to Malawi. What Mpwiyo did is not different from murder. He needs full remand!

Uchitsiru Sasekana
9 years ago

Chachikulu apa A Malawi tisiye kaye kudulidwa msonkho Boma libweze ndalama zones zobedwa kuthumba lachitukuko kuti tonse tipindule ndithukuta lomwe timakhetsa tsiku ndi tsiku usana ndi usiku apo BIII Zivuta pa Malawi

pearson sadala
pearson sadala
9 years ago

Lloyd amapita kukamwa ma whisky kunyumba kwa mphwiyo . What do you expect

Ken nsonda
Ken nsonda
9 years ago

Iye mphwiyoy osadabwa kuti sanafe after zipolopolo zitatu kuba kwao mulungu anakwiya nako and mulungu samalora imfa ya munthu ochimwa hahahahahahahaha ali kaka anawombera kamodzi munthu pompopompo ku duwa usova aise lero ife pa afrikaans umodzi umodzi.

chilungamo
9 years ago

Guys why do you want a Mlakho judge to preside over Mphwiyo who is also a Mlakho? The judge has done well to recuse himself, let a neutral judge without any connections to any political party preside over this case! We have capable judges who can do this job. Muhara has done well to recuse himself I hope this will also have a ripple effect on the other judges from that other region who shield and defend each other.

Njolinjo mwana wamama
9 years ago

Mbaya!!!, mwee!!, they’re on it again! It’s either sickness or some Judge is recusing himself/herself out. Or we need here is justice. Majajiwa akufana kudya nawo chabe apa, choonadi akuchidziwa.

Mphembedzutsokonombwe
9 years ago

Kodi onse amene amamangidwa ndi kuwakaniza bail siwanthu! iyeyu amadya ndalama ngati masuku pamodzi ndi mbava zina zones za Cashgate ayenela awone m’mene ndende imakhalira!

Frenzo
Frenzo
9 years ago

Anthu ambiri anafa chifukwa cha Luba kwake mphwiyoyo ndiye uziti his life is in danger ya chiyaninso? Tinampatsa kale bonus anatibera komanso kuononga ndalama zambiri ku chipatala. He should now dance to the music he enjoyed playing

cameroon
cameroon
9 years ago
Reply to  Frenzo

Ndipodi akati his life is in danger, how special is he? Isnt he the image of God like us? How many are suffering in the cells with petty issues and how many died due to lack of medicine? Timve zenizeni!!

Makwale
Makwale
9 years ago

muhara anene chifukwa

Read previous post:
Osman set to fix Mighty Wanderers

Mighty Wanderers Technical Director, Yasin Osman, says he will  iron out the club’s teething troubles he sets about “rebuilding” the...

Close